Zokonda AMAYI NDI Abambo

Zokonda AMAYI NDI Abambo

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zokonda AMAYI NDI Abambo, Health/Beauty, Blantyre.

01/05/2023

Phoni yako ili mmanja choncho yamikani mulungu chifukwa anzako ena akuthatha ndi IFA ena ali pa OXYGENπŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ™

Photos from Zokonda AMAYI NDI Abambo's post 22/04/2023

Catholic university why?

21/04/2023

Zachitikanso ku CU Rodger naye uku..... Send number zisakudutseni nebah

20/04/2023

Admin post for me

Am Lucy banda, 24 years old komanso ndili ndi degree school ndaphunzira ine si mzamakwalala and am not cheap as you think chifukwa ndapanga post pano no am graduate

Ndusaka mamuna koma akhale oyera, wa galimoto kwawo kolozeka osati ku kuchigumbu komanso adziwe ndili ndi mwana m'modzi wa dzaka 12, sikuti ndikusaka banja kamba kovutika no but am tired ndizofusilidwa ndi a sasamba any interested apezeni admin

20/04/2023

Admin help me

Ndikusaka mamuna wa banja koma akhale serious, ndili ndi ana atatu ndipo ndikufuna mamunayo akhale wapa ntchito yabwino osati business akhalenso munthu okuti ali malo kale samasowa ndalama sindikufuna ana anga adzazuzike

17/04/2023

Admin please post for me

Azimai kod is it normal mamuna mpaka kumakugona 12 rounds pa day kapena zina zangokhala nkhaza chabe??😭😭😭

14/04/2023

Azibambo izi ndi nkhaza, kumenya mpaka kuchotsa Mano mmmh

10/04/2023

Mamuna uyuyu sikudziwa kuti amakhala kutiko. Koma Ali pa page pompano ndimawona ma comment Ake, saname ndatopa kuzisunga mutima zokhumba zanga. Ngat suli pabanja komwe uliko dziwa kuti admin ine ndakukonda ndiwe handsome ungathe kundibelekela mwana owoneka bwino ngati iweyo

Ngat uli pabanja vuto palibe utandifunisisa tingathe kumangozembelana bola mwana yekhayo utandipasa or osasamala ndekha ndingathe kumusamala umandisangalasa sakubisile ndipo kumbali yayine usawope ndili singie.
Banja langa Latha mwezi wathawu chowopsa palibe osawo.

Ndili kuno kulilongwe please ukawona post yangayi ungathe kumasuka nane, koma ngati sunandifune vuto palibe sizokakamiza. Ndiwe owoneka bwino dear admin ndagoma nawe

10/04/2023

Good morning πŸŒ„

18/03/2023

Hide my l'D admin

Uyu ndi mkazi wa mzanga ndipo Anthu wa akhala dzaka ali pa banja koma momwe ndimawonera samakondana two months ago mkazi yu anapita ku mudzi kukaona mayi ake koma sim'mene mzangayo amapanira mahule

Mkazi wake atabwera mzangayo sanasinthe khalidwe ili ndipo zinandinyasa kwambiri poganizira kukongola kwa mkazi wake

Ndufuna akaona nkhani yi mkaziyo adziwe kuti akungotaya nthawi samamukonda ndipo mamuna wakeyo ali ndi akazi ambili mwinanso 5 akwana

Ndi bwino usafele banja mapeto ake akumaliza si munthu wabwino mamuna wako uja uchenjele zoipa zisanakupeze pakira malo okhala sangasowe ife monga amzake amunako tikuthandizani osakaika

Uthengawu zandivuta kuti ndikupezeni ndi mkana ndaganiza njira yachidule kubweletsa pano

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Blantyre