CHABE GANGS

CHABE GANGS

Share

Malawian Gangsters, we sort out the country in peaceful manner

Photos from CHABE GANGS's post 01/04/2026

Munthu wina osadziwika, anaba galimoto ya mtundu wa KIA Sorento pafupi ndi malo othirira mafuta pa Kudya ndipo amayendetsa galimotoyo mothamanga kwambiri kulowera nseu wa Sanjika.

Ndipo adaomba chipata chili pafupi ndi sanjika, pothawa wakaomba galimoto ina Ford Everest pafupi ndi ofesi za MRA.

Galimoto yobedwayo zuoneka kuti munalinso mwana kumbuyo ndipo info yonse atanene ndiapolisi akuchilomoni amene amutenga munthu akukayikilidwa kuba yo.

22/02/2026

Kamangila akupenga do not entertain him.

08/11/2025

Fuel
Forex

08/11/2025

I don’t hate Peter komano akutani dziko lino? Mafuta azisowaso chonchi

08/11/2025

Fuel akuvutaso why

08/11/2025

Dziko Lino limangofunika kupha Aliyese yemwe anadyapo ndalama za misonkho yathu

16/10/2025

MK1

13/10/2025

Sad truth

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Kuilsriver Capetown
Blantyre