Kulinj Lucius
Hard work
14/09/2022
A MUTHARIKA AJA MUSAWAMVERE, SANGATITHANDIZE PA MAVUTO AWAWA-watero katswiri.
Katswiri yemwe amayankhulapo pankhani zosiyanasiyana, Latimu Matenje wati zomwe mtsogoleri wakale wa dziko lino, Professor Peter Mutharika wayankhula dzulo ponena kuti ulamuliro wa Tonse Alliance uthetsedwe mzopanda mchere kwenikweni.
A Matenje ati zikadakhala bwino a Mutharika akadagwilitsa ntchito msonkhano wawo wa dzulo pobweretsa poyera mfundo zomwe zingathandize kuti dziko lino lichoke mu singa za umphawi.
Katswiriyu anaonjezera ponena kuti ngakhale boma lomwe liliko pano likulephera kupanga zakupsa, izi sizikutanthauza kuti anthu ena, kuphatikizapo a professor Mutharika awonekelepo ochenjera.
Powonjezera, katswiriyu anati ena mwa mavuto omwe dziko lino likudutsamo akhala ali a m'gonagona, zomwe akuti sizoyenera kulozelatu chala ulamuliro wa Tonse Alliance pansi pa Dr Lazarus Chakwera.
Komabe, katswiriyu wati mkofunika boma la khwimbi la zipani pansi pa mgwilizano wa Tonse lizindikire kuti pofika lero likuoneka kuti nalonso lilibe mayankho pa mavuto omwe akuta dziko lino.
Dzulo, mtsogoleri wakale wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha Democratic Progressive, Peter Mutharika anagundika kuloza chala ulamuliro wa Dr Lazarus Chakwera ponena kuti walephera kulamulira bwino dziko lino.
Mwazina, a Mutharika anati mkongofunika a Chakwera atule pansi udindo wawo mkulolera kuti dziko lino likhalenso ndi chisankho china mkatikati mwa miyezi itatu.
(Newsroom)
04/09/2022
Malawi Flames lineup 🆚 Mozambique
Brighton Munthali
Stanley Sanudi
Paul Ndhlovu
Miracle Gabeya
Gomezgani Chirwa
Yamikani Chester
Chimwemwe Idana
Micium Mhone
Chikoti Chirwa
Schumacher Kuwali
Chiukepo Msowoya
04/09/2022
It's mawa odi ukoooo ku Ndilande
Nyabadwe School Ground....
👌👌👌
04/09/2022
02/09/2022
Bungwe la CAF likudziwitsa anthu onse kuti anthu okwana 40000 ndi omwe akawonelera masewero pakati pa ma team a Nyasa Big Bullets ndi Simba SC mu mpikisano wa CAF Champions League.
Masewero wa adzachitika pabwalo la BNS mu mdzinda wa Lilongwe pa 10 September 2022.
Mkulu oyendesa ntchito ku team ya Nyasa Big Bullets, Albert Chigoga wati ma tickets olowera ku masewero wa ayamba kupezeka mawa lachisanu...
02/09/2022
Tinali komko Ku Blantyre High Court,M'malo mopanga terminate case,angopanga reduce sentence from 8 years to 3 years,mukamapeleka chigamulo muzidziwa kuti kubeleka ndikowawa mokuti nane ndinafika polira ðŸ˜ðŸ˜nditadzadzidwa ndi chisoni poganiza za sentence ya M***a John komanso powawona Mayi Ake a M***a John akulira, guys Mastein Ake a M***a John sikuti ndi olemela mokuti ngati Pali mfana Modzi amene amawathandiza ndi M***a,guys tiyeni tiliyikize M'ma Pemphero banja limeneli lakwa M***a John kuti MULUNGU Alidalitse, Mazibusa komanso aliyense wakufuna kwabwino tikuyenela kumakamuona M***a, komanso Mayi ake kumakawalimbikitsa kupemphera.May GOD be with You and BLESS Your Family, MULUNGU amapanga njira popanda njira ndili ndi chikhulupiro kuti utuluka
02/09/2022
Mu Gheto Ndilande 3 days to Go....
Nyabwadwe Primary school Ground.
02/09/2022
Our Dear President Dr Lazarus Chakwera , I strongly believe that you are a caring father full of love and compassion.
As a nation particularly the youths, we are crying and begging you to act within your stipulated powers to pardon the young boy M***A JOHN who has been sent to prison for reasons better known to the prosecutor and Judges.
Your Excellency, I am not in anyway condoning lawlessness because "a crime is a crime" regardless of who commits it, BUT SELECTIVE JUSTICE IS EQUALLY EVIL and that's why we are standing against it without fear.
Similar cases have been dealt with differently in our courts and all the offenders were given a FINE option including a South African Truck driver who was found with many bags of the same CHAMBA but how come M***A JOHN is being treated harshly? and the courts have been so quick to throw this young boy to prison without giving him an opportunity to pay a FINE?
Mr. President Sir, assuming your page is managed by someone else or if at all you have advisors who cares about your legacy, I beg of them to pass on this humble request to you your Excellency to free M***A JOHN on presidential pardon.
Bwana President, anthu osawuka omwe chiyembekezo chawo ndi inuyo ndipo tikudziwa kuti mumawayika pamtima panu...Lero misonzi yawo yasanduka nyanja yosowa powolokera. Tichitireni chifundo, mumasuleni M***A JOHN.
Ndatha ine mwana wanu
Thocco Anaphi KatimbaðŸ˜ðŸ˜
02/09/2022
Zatsimikizika kuti ndende zaku Malawi mkokhala anthu osawuka, ndipo zoonadi amphawi alibe mawu.
Koma tsiku lina misonzi ya amphawi idzasanduka nyanja yovuta kuwoloka.
Zavuta pati kumupatsa FINE kuti alipire monga mumachitira ndi ena achuma aja? Olo mukanati 10million uyuyu tikanasonkha kuti atuluke.
But One Day is One Day, misonzi ya anthu osawuka idzapanga nyanja yovuta kuwoloka ndipo ichi chidzakhala chipasu-pasu.
My Heart is really broken 💔 ðŸ˜ðŸ˜
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Lilongwe Area 14
