Mlakatuli kelian Mnzindo

Mlakatuli kelian Mnzindo

Share

For entertaining

21/07/2022

ine
Mnyamata aliyese alindi zibwez kuyambira ziwiri kumapita mmwambamo...tizibwez tako tonseto tinkhala ndi Mimba(pregnant) kumayambiliro kwa August
πŸ™„πŸ™„πŸ™„πŸ™„πŸ™„ Amen kumpando

14/07/2022

friend
1:munthu amene amadziwa zofooka zako km osakupanga chipongwe mkonden ameneyo
2:munthu amene amakuthandiza ukapeza vuto mkonden ameneyo
3:munthu amene amakudzudzula ukalakwitsa mkonden ameneyo
4:munthu yemwe samasangalala mukamadandaula mkonden ameneyo
5:munthu yemwe amakuwunikila za tsogolo labwno mkonde ameneyo
6:munthu yemwe amakulimbikitsa makhalidwe abwno mkonden ameneyo
Same thing to me ndkondeniso
my PageπŸ™πŸ™πŸ™

06/07/2022

Nkhalidwe ndichumaπŸ’₯
PART 1
John:koma madolo mukudziwa chn apapa tisute bhobho then tivaye kwa beab inja....John ndazizake anagwrizana kufikapanja pakt makolo awo samadziwa zomwe anawo amachita ngakhale anthu amawawuza makolowo km sankawavera amkangoziponya kunkhongo kufikila tskulina anakumana ndi amfumu amudz mwawo ndipo znali motele

Say next ku page iyi kt ipitilile ngt silibh munenaso

06/07/2022

Kukulolan lero mawa akt akwao amuza kt mumukwatile πŸ™„πŸ™„πŸ™„πŸ™„πŸ™„

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address

Lilongwe