Msungwi Whatsapp group Page
Reading & Listening Music
16/06/2025
It was Chiwamba Health center in Chiwamba
16/06/2025
LILONGWE AREA 25,MSUNGWI CHARITY GROUP...
MSUNGA PRIMARY SCHOOL M'BWATALIKA
16/06/2025
MSUNGWI CHRITY GROUP
KUGAWA SCHOOL INFORM @ MSUNGA PRIMARY SCHOOL M'BWATALIKA
16/06/2025
16/06/2025
MSUNGWI CHRITY TRIP
KUGAWA SCHOOL SCHOOL INFORM, MSUNGA PRIMARY SCHOOL M'BWATALIKA
07/03/2025
📢 DZINA MWA ZOMWE WANENA JB PA ZODIAK EXCLUSIVE
1️⃣🏠 "President Chakwera tinakumana pomwe ankandisankha kukhala ambassador wa goodwill wa za Cyclone Freddy. Anatiuza kuti adzatiitana kuti tikakambilane za budget kuti timange nyumba za anthu, koma mpakana lero. Moti ine nyumba zomwe munkaona ndimayendera zamangidwa ndi Joyce Banda Foundation."
2️⃣💰 "Chuma cha dziko lino sichikuyenda, pali mavuto. Chiyambileni, katundu sanakwerepo katatu pa tsiku, 1 dollar mpakana kumagulisidwa 5,000 Malawi Kwacha. Ngati dziko tikufunika kupeza njira zoti tipedzere ndalama zakunja."
3️⃣🌱 "Amene ankakamba za ma Mega Farm ndi Saulos Chilima, a Chakwera ankakamba za High 5. Green Belt ili kuti? ADMARC ili kuti? Chifukwa Green Belt bwenzi ikutithandiza kulima chakudya chokwanira."
4️⃣🚔 "Ukakhala president zambiri sumadzidziwa zikamachitika kunja, chifukwa kunjaku anthu amatakata (kuba/katangale). Nde ukawadziwa umawachotsa ntchito ngati momwe achitira President Chakwera. Ena amafunika kumangidwa kuti azikuopa, so Ukakhala kuti nawe so ndiwe wa katangale, nde amakuophyeza kuti tikuwululani."
5️⃣📉 "Kuti zinthu ziyende m'Malawi muno, tikufunika tithetse kaye katangale, komanso tipeze forex."
6️⃣🌍 "Ubale wathu ndi maiko akunja sikuti unaipa. Nthawi yomwe ndimalowa ine, mpamene ubale sunali bwino. Tonse tikukumbukira kuti dziko la Britain ubale tinathetsa (titha kupempha maiko akunja kuti atithandize kupeza forex)."
7️⃣🏗️ "Ndikudabwa kuti nyumba zomwe ndinamanga ine through Joyce Banda Foundation zikupezeka mu SONA, watiyezeka."
Mneneli wa chipani cha UTM a Felix Njawala ang'alula mkulu wa MBC a George Kasakula kuti akusamalika ndi MBC ngati yakunyumba kwawo ponyoza atsogoleli azipani zotsutsa kuphatikizapo UTM ndi DPP.
Mchikalata chomwe a Njawala alemba adzudzula a Kasakula kuti iwo siwoyamba kugwiritsidwa ntchito molakwika Ku MBC. Akuti anzawo analiponso koma lero ntchito inawathera.
28/02/2025
Rest In peace Witwas
Kwathu Sipa Dziko
28/02/2025
REST IN PEACE
MSUNGWI WHATSAPP GROUP ILI PA CHISONI,
Ife agulu LA msungwi whatsapp group taluza mmodzi mwa mkulu yemwe adayamitsa nawo guli.
Witwas last on Anali mmodzi mwa munthu yemwe adapanga gulula msungwi kufiikira muzinthu zambiri.
Mzimu wa Witwas Ukawutse mu mtendere.
Click here to claim your Sponsored Listing.
