Nkhani Za M'maboma
πTHIS IS THE LATEST & FASTEST GROWING PAGE FOR BREAKING NEWSπ . Welcome πkuing'alura osaopaππͺπͺ
10/04/2026
NKHANI YOMVETSA CHISONI KWAMBIRI ππ
Pa nseu wa nguludi odzera mminda ya kwa kamwana muboma la Dowa pa trade ya Mponera kwapezeka mai waphedwa alindi mwana kumbuyo imagine kumupha munthu wamayi mwana ali ku nsana ππ
Malemuyu anali ndi ID pali zina lokha ndilomwe likuwoneka bwino,zonse pa ID sizikuwoneka bwino bwino.
Zina la malemuwa ndi Ida kamumwamba.
Mwana wa amalemuwa Ali moyo .
Nkhani yik*t eni munda anatuma ana atchito k*t akatcholeko ndiwo kumunda,anyamatawa atafika kumunda anapeza mwana akulila mmunda momwemo. Atayang'ana anapeza pali mayi koma atafa kale mwana alimusi mwa chitandacho akulira.
Apa ndipo anyamata aja anapita kumuzi kukauza anthu zangoziyi.
kwawo kwa malemuwa sikuziwika
Pempho zinthuzi zachitika dzulo madzulo ππ
Ngati ukava Dzina la
Mulungu limakubowa
Dusa
Usalembe AMEN ππππππππππππππππ
07/02/2026
Ambuye adaliseni awaπ Asitheni nyengo zawo Ngati akwanise kulemba amen ndikupanga gawa uthengawu kumagulu awoπ( MULUNGU NDI MATHERO AMAVUTO ONSE)
Nkhan
Apolisi m'boma la Ntchisi atsimikiza za imfa ya mwana wa miyezi inayi, Alexander Chimpeni, wa m'mudzi mwa Chiwembu m'bomalo yemwe wamwalira mayi ake atamugwera pomwe amamenyana ndi munthu wina.
Malingana ndi m'neneri wa polisi m'bomali Salomy Zgambo wati patsikuli mayiyu amakangana ndi nzawo atamubeleka Alexander kunsana ndipo ali mkati mokangana ndewu inabuka pakati pa awiriwa ndipo mwatsoka mayiyu anagwa ndik*tsamila mwanayu.
Zgambo wati zitatero anathamangila naye ku chipatala cha Ntchisi komwe achipatala anatsimikiza k*ti mwanayu wamwalira.
Zotsatira za chipatala zawonetsa k*ti mwanayu wamwalira kaamba kovulala kwambiri m'mutu.
Wolemba: Maureen Kanyundo
NKHAN YONGOTIPEZA KUMENE
Masewero apakati pa timu ya Malawi ndi Equatorial Guinea alepheleka kamba ka zifukwa zina.
Masewerowa amayenera kuchitika pa bwalo la Bingu National munzinda wa Lilongwe usiku wa lero.
Koma malinga ndi kalata ya bungwe la Fam, masewerowa alepheleka chifukwa timu ya Equatorial Guinea yalephera kufika m'dziko muno.
Tikupatsilani zambiri posachedwapa.
Wolemba Mabvuto Kambuwe
Ndani ak*ti Kumwamba kwamukondera wadzuka ndi MoyoβοΈ
π
Ngati umakhulupilira k*ti Mulungu tsiku lina adzasintha nyengo za moyo wako
Tangolemba AMEN
Ndikugawa uthengawu kuma group atatu
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Luke Nkhoma, Hendreson Banda, Felister Kapalamula, Tiyamike Lameck, Tamala Chaula, John Enock, Hannah Julius, Rombani Zulu, Chiku Wastaubi, Gomani Mw, Glady's Nikell Kabvina, Manzy Mwanyada, Washington Mtaghayo, George Mussah, Preciuos Jalison, Sailess Steve, Stephano Daniel, Rajji Chiyenda, Chenje Ethel, Julius Chionetsero Maulana Maulana, Phelisters Shemmah, Davie Makina, Dyson Innocent Chitwanga, Eliz Ndenda, Mathews Lozalio, KONDWAN CHINYAMA, Aubrey Ziwoya, Joseph Moyoh, Usu Dip Samu, Austin Mataya, Stephan Stephen, Anessa Mwangiwa, Lazalo Felix, Bles Mwale, Makwinja Kassim, Jefule Jefule, Mandala Chirwa, Maseko Phili, Danger Manyika, Watson Mwale, Mangwanje Mbewe, Promise Michael, Emran Balakas, Shafi Kassim, Pemphelo James
ZINA UKAMVA πππππ
Anyamata awiri omwe pakadalipano sakudziwika mayina awo apezeka atafa mam'mawa uno pafupi ndi malo okwelera minibus zopita mu Limbe omwe ndi oyandikana ndi nyumba za Blantyre Water Board komwe ndi kuseli kwa Kamuzu Stadium.
Anthuwa omwe matupi awo akuoneka ndi zilonda komanso magazi akuganiziridwa k*ti achita chophedwa ndi anthu okwiya atagwidwa akuba zipangizo za khebo za lamya pamalo omwe ali pafupi ndi pamene afera pomwe paonetsa k*ti anali atayamba kale kudula ma khebowa potengera k*ti mmanja mwawo mukuonetsa atavala zozitetedzera (gloves) zomwe anavala munthawi yomwe amayamba kuchotsa zipangizozi.
Ndikuona anthu 1000 on this page Mulungu ak*tembenuza nyengo zawo kukhala umboni wachimwemwe, mu dzina la Yesu ChristπποΈποΈ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Website
Address
INVITESOTHERSTOLIKETHISPAGEOF
