Lilongwe UTM Vendors

Lilongwe UTM Vendors

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Lilongwe UTM Vendors, Health/Beauty, Lilongwe.

03/09/2025

Chiyembekezo chopambana chisankho chili pa 90% serious utm ikulamula dziko pa16

29/08/2025

Ngati uli dolo dziwa ndiwe wa UTM

Ngati wosamba dziwa ndiwe wa UTM

Ngati ndiwe oganiza bhooo ndiwe wa UTM

24/08/2025

Kwa ife Chipani ndichomwechi sitikusintha

Photos from Lilongwe UTM Vendors's post 18/08/2025

Dr Dalitso Kabambe writes

Dr. Bingu Wa Mutharika came to power through UDF, koma atawona vision yawo, anawona kuti ku UDF sangakwanitse kuzikwaniritsa and so, he had to go elsewhere where his vision and institution blend with the vision and for Bingu, anayambitsa DPP, yomwe anayipatsa culture yomwe iwowo ankayifuna.

Dr. Saulos Chilima anayambira ndale zawo ku DPP, koma later anawonanso kuti masomphenya maka othetsa katangale, tsankho lamitundu, ma reforms, sizingatheke pansi pa DPP, he moved on to form UTM.

Ine ndinayambira ndale ku DPP, tinayesayesa koma tinawona kuti ayi tisunthe. Sindinangofikira kulowa UTM, ndinayang'ana zipani zambiri, their mission statement, culture and values, ndipo ndinawona strong desire from UTM to end corruption, nepotism, reform government system, bring innovation and develop Malawi, I was convinced UTM is the right place to be.

Ndikunena ichichi ambiri timatsatira zipani mchimbulimbuli, kuwafunsa kuti awa mmawasapota chifukwa chani, munthu wa degree, masters or PhD imene amakanika kuyankha, chomwe angakuwuzeni nkuti ngwa ku Ntchisi, Dowa, Mulanje, Thyolo, Rumphi, Karonga. So, ophunzira ndi osaphunzira osasiyana.

I want to challenge everyone here, politics is life, kuchipatala kulibe mankhwala a TB, ma patient a TB ngati sakulandira mankhwala next thing ndi imfa, imfayo sisankha kuti awa ngakudedza musawaphe, iphani aku Phalombe, tonse tifa. Njala siwona Mchewa kapena Mtumbuka, imapha aliyense chimodzimodzi ilibe tsankho

Tiyambe kuwona ndale in line with our lives komanso dziko. Tikupindula chani, dziko likuyenda bwanji, titsatire chipani chomwe chili nkuthekera kofewetsa miyoyo yathu komanso kutukula dziko lathu.

Amati, you can't get different results by doing same things that failed. Pangani chisankho chopanga join this movement, for the sake of Malawi. Our country is bleeding, anthu akufa muzipatala, 65% ya imfa zathu timafa because of failed health systems. Abale athu ambiri analowa mmanda osati nthawi inakwana, koma tinalephera kuwasamala. UTM i

14/08/2025

Dr Dalitso Kabambe sakusankha akutenga aliyese chifukwa wabwera kudzasintha Malawi

14/08/2025

Ulendo waku 16 kuti UTM ilamulire ukupitirira motere

09/08/2025

Our National Youth Director Hon Penjani kaluwa Fredokiss wil join this panel Discussion.

Photos from Lilongwe UTM Vendors's post 09/08/2025

UTM Presidential running mate also the next Vice President of Malawi, Hon Engineer Dr Mathews Mtumbuka omwe aperekezedwa ndi Hon Yongo Wa Yongo UTM's National Director of Strategic Planning mamawa uno ali nawo pa mwambo wa maliro ku Rumphi wa omwe anali m'busa wa CCAP ku Livingstonia Synod malemu Rev. I.V Gondwe. Nzimu wao unse mu mtendere 🙏

08/08/2025

Dr Mathews Mtumbuka nayetu sakugona tulo

07/08/2025

Dr Dalitso Kabambe central region watekesa hvy

05/08/2025

Tikutipula sure

01/08/2025

Ntchito ya bwana Dr Dalitso Kabambe ndi imeneyi lero

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Lilongwe