Proudly Mzuzu City Organization

Proudly Mzuzu City Organization

Share

Keeping Mzuzu City always clean

26/02/2026

Mzuzu mzuzu mzuzu 😍
Okay bweran apa tiyankhulaneπŸ€—

Tikusaka anthu awiri, wabambo ndi mayi koma akhare osachepera dzaka 25 kapena kudutsa 35 omwe angathe kukhara achifundo Komanso kutha kuyendetsa ntchito zachifundo.

Please tiyankhulen ku inbox ngati mlinako kuthekera
Okhao alimdera la Mzuzu city

24/02/2026

The only help you need right now πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

14/02/2026

Wina kuno... πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚
🀣🀣🀣🀣

14/02/2026

🌹🌹
So mwati Inu za Valantines simpanga nao kapena vuto mkumakumana ndiachikondi ofuntha okha-okha...πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

11/02/2026

Good news...!!!
... Mzuzu.... MzuzuπŸ’β€οΈ

Okay tabwerani tiyankhulane... πŸ€—πŸ€—

Kuyambira pa 01 March 2026, Tiyen tizipeza Malo amodzi around our green city .
Eg,(1) Ma drain, Ma health centers or mzuzu central, MA potholes in our roads and many other places fix it (Around mzuzu city only)
(2) kupeza omwe Ali aukalamba kapena olumara ndikuwathanza mwazina zomwe zingatsintheko miyoyo Yao!
(3)Kupeza Ana amatsiye kapena ovutikitsitsa omwe sangathe kuthekera kupeza Zina mwazithandizo za school like Uniforms, books and more.

We can do more to change the lives of many who are in need... πŸ˜˜β€οΈπŸ’
Let's go

11/02/2026

SAKEDπŸ€—πŸ™„

11/02/2026

With Zodiak Online – I just got recognized as one of their top fans! πŸŽ‰

11/02/2026

With Podcast Malawi – I just got recognized as one of their top fans! πŸŽ‰

09/02/2026

My Malawi wake up please 😒😭
Kufana Omupembeza koma kaganizidwe kotsiyana... πŸ™„πŸ™„

Photos from Proudly Mzuzu City Organization's post 08/02/2026

Ambiri akhumudwa ndikulemba kwa ATelo(Mwiza-The life coach 😎😎


-uyu our own mzuzu sister naoso wayooyapo mwamahalako ndithuπŸ€“πŸ€“πŸ€“πŸ€—πŸ€—

☺️☺️☺️

Website