ibn ja'far
to grow up our communication with Allah
Eti zafika pomafusa kuti nkhondoyi wawina ndi ndani kkkkk
koma ma super power enawa
Koma kwabuka ti ma sheikh pa social media mmmmm
05/08/2025
ad-dajjal uja aku trenda uku takaoneni
TikTok · ibn ja'far 6279 likes, 442 comments. “dajjal part 1”
Dajjal part 1
I'm ready
Are you ready for ?
Step iliyonse ya munthu Allah amailondoloza bwino kwambiri, koma mwini sitepeyo kuchita tchimo mopanda manyazi
Mulungu atikhululukire
Mukazamuona ali cheeetee zasiyeni kuyankhula, amakhala kuti wanvetsetsa, kwinako mungazaononge.
Mwanva azimayi???
Mwachitazo sizabwino musaziikire kumbuyo
الحمدلله الذي أحيانا بعد ما أمتنا وإليه النشور
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Salima
