Ungwazi
Nasanganya wazinthu
kuchimpwilikiti
kumpanipani kwenikweni
Anthu anga okondedwa ndiuzeniko amene mukuzimvetsesa bwino๐ค
Follow Ungwazi
25/06/2026
Uyuu ndikodzi mwaanthu omwe akuchokera kujohn pama bus aulele anthu ena akutha mawu koma ena akuti munthuyu akufunika thandizoโค๏ธ
Kwanthu onyoza muziziwa kuti lungalunga nkubadwa chilema chiza kuukulu anthu ena anapita kujoni alibwinobwino koma analumala ndingozi zosiyanasiyana Ambuye amuthandizire bale wathu ineyo yemwe angamupezeko chonde mundilumikizitse kangachepe komwe ndingapezeke nako ndimuthandiza kwaomwe mukukhuzidwatso tithaso kupanga chimodzimodzi Ambuye akudalitseni๐๐
FOLLOW Ungwazi
Zojamburana sizabwino pliz chonde๐๐
Follow Ungwazi
Kodi ku amalembaso obwera ngati? Zalowa ntchimpwilikiti
Follow Ungwazi
23/06/2026
Ayii zikomo๐๐
Follow Ungwazi
Amalawi omwe amathawa zipolowe kuSouth Africa apanga ngozi kumashingo (Masvingo)awiri amwalira ena avulala ๐
Follow Ungwazi
22/06/2026
ZOMVETSA CHISONI ABALE NGOZI YOMWE WAPULUKA NCHIMWENE G WISE YATITENGERA MALU MALU ๐๐๐ญ
Amaziwika kwambiri ndinkhani yothandiza amalawi okhala ku South Africa kupangisa mapepala okhalira mzikolo
Rest in peace brother ๐
Koma chomanyamulira ma HD camera mu stadium ndichani mwati?๐๐
Mpake situkufuna kubwera mukumangojamburana osafunsa kaye ๐
20/06/2026
Abale tiyeni tizipita kulibwino ukafike mphawi kumalawi ulindimoyo kusiyana tikafikire muma casket odura aboma tili ntembo๐๐พ
Amalawi 7 aphedwa zulo nziko la south Africa ku Durban ndi gulu lotchedwa march to march lomwe lavuta kwambili nzikolo.
Malingana ndi mareport omwe taona anthuwa anayamba kuyenda munseu ndi mmakomo kudera la Pietelizburg ndipo akapeza obwela amamenya kukhapa komanso kupha kumene.
Pachiwembuchi amalawi omwe afa ndi 7 ndipo ochulukirapo avulazidwa kwambili ena mwaiwo anathawisidwa ndi Apolice pa nthawi ya ziwawazi.๐
Follow Ungwazi for more news
Koma zowona izi abale?
Follow Ungwazi
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Mzimba
......
