The Rez Nation TV

The Rez Nation TV

Share

β€œlaugh till crying” πŸ˜‚πŸ”₯πŸ™Œ
New page, support me guys.πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡ΏπŸ‡²πŸ‡ΏπŸ‡¦πŸ‡²πŸ‡Ώ πŸ‡ΏπŸ‡ΌπŸ‡°πŸ‡ͺ

22/03/2026

POV: You try to surprise your wife and she activates self-defense mode 😭πŸ”₯

"Laugh πŸ˜‚ until crying"😭

New page, support me guys πŸ™ πŸ˜‚

22/03/2026

When you try to be the craver one… but she’s already ahead πŸ˜…πŸ”₯

New page, support me guys πŸ™ πŸ˜‚

22/03/2026

β€œWen you Married to a man who never takes anything serious πŸ˜†πŸ”₯”

β€œ laugh till crying πŸ˜‚πŸ”₯”

New page, support me guys πŸ™πŸ˜‚

22/03/2026

When she finds cheating messages in your phone… pray for yourself πŸ˜‚

β€œOnly legends will laugh till crying πŸ˜‚πŸ”₯”

New page, support me guys πŸ™πŸ˜‚

21/03/2026

Breaking news πŸ“° πŸ“• πŸ“Ί πŸ”₯

Anthu angapo omwe akukhala m’dziko la South Africa popanda mapepala ovomerezeka agwidwa ndi akuluakulu a boma pa nthawi ya chikondwerero cha Eid Mubarak.
Malinga ndi malipoti, anthuwo anapezeka ali pa msonkhano wokondwerera Eid, komwe akuluakulu a chitetezo ndi a za immigration anachita opareshoni yofufuza anthu osaloledwa kukhala m’dzikolo.
Zikudziwika kuti ena mwa anthu omwe agwidwawo ndi ochokera ku Malawi, ngakhale chiwerengero chenicheni sichinatchulidwe.
Akuluakulu akuti opareshoniyi ndi gawo la kuyesetsa kulimbikitsa malamulo okhudza kulowa ndi kukhala m’dziko, ndipo anthu omwe apezeka alibe zikalata akuyembekezeka kupita nawo ku malo osungiramo anthu osaloledwa asanabweretsedwe kumayiko awo.
Boma la South Africa likupitiriza kulimbikitsa anthu onse obwera kudziko lino kuti azitsatira malamulo ndi kukhala ndi zikalata zovomerezeka.

ENGLISH:πŸ“°πŸ“•

Several undocumented immigrants were arrested in South Africa during an Eid Mubarak celebration.
Authorities conducted an operation at the gathering, where they discovered individuals without valid permits. Some of those arrested are reportedly from MALAWI.
Officials say the operation is part of ongoing efforts to enforce immigration laws.

21/03/2026

Breaking news πŸ“°πŸ“•πŸ“Ί

Mkulu wakale wa MALAWI Immigration a Charles Kalumo aopseza bwalo lamilandu kuti ngati siliwapatsa bello ayambilanso kunyanyala chakudya.

Kalumo anamangidwa lachitatu akuchokela ku South Africa ndipo pano ali kuchipatala china mumzinda wa Lilongwe kumene akulandila thandizo moyang'anilidwa ndi apolisi.

ENGLISHπŸ“°πŸ“•

Former Malawi Immigration Chief Charles Kalumo has threatened the court that if he is not granted bail, he will resume his hunger strike.
Kalumo was arrested on Wednesday upon his return from South Africa and is currently admitted to a hospital in Lilongwe, where he is receiving treatment under police guard.

The Rez Nation TV

21/03/2026

Eyes can lie πŸ˜… this guy was pretending to be a woman…uyu amubathaπŸ˜‚πŸ˜‚

β€œLaugh now, cry later πŸ˜‚ stay sharp!πŸ˜‚πŸ”₯”

New page, support me guys πŸ™πŸ˜‚

21/03/2026

Zakazaka wampalamula mponda matikiπŸ˜‚ ulemu wanu mr kamkudzukudzu Passover Channel With Zaka πŸ‘‘πŸ™

β€œOnly legends will laugh till crying πŸ˜‚πŸ”₯”

New page, support me guys πŸ™πŸ˜‚

21/03/2026

β€œOnly legends will laugh till crying πŸ˜‚πŸ”₯”

New page, support me guys πŸ™πŸ˜‚

21/03/2026

Imfa iweyoπŸ˜­πŸ™

Photos from The Rez Nation TV's post 21/03/2026

SAD NEWS ( South Africa )

Akasia, outside Pretoria; R566 Rama City behind Sefako Makgatho University.

Rocks are being placed on the road. Three people died after they crashed head-on into a truck
trying to avoid the rocks.

Ku Pretoria dera lotchedwa AKasia ku nsewu wa R566 kuseli kwa Sefako Makgatho University kwada anthu atatu omwe alipachithunzipa,

Malingana ndi malipoti akuti anthu osadziwika bwino akumaika miyala pa nsewu kuti odutsa ndi magalimoto azigwa moti anthu atatuwa amwalira pomwe amazemba miyala yo galimoto zawo zinagudubuka ataombana ndi truck pomwe amayesera kuzemba miyala

The Rez Nation TV πŸ“Ί

21/03/2026

NKHANI ZOPATSA CHIDWIπŸ˜’πŸ™Œ

Zigawenga ziwiri zapasidwa chilango chokakhala ku ndebe moyo wonse, chifukwa chopha mkazi wa zaka 21 yemwe anali ndi pakati (miyezi 8). Mumzinda wa Cape Town

Mayi, Shahieda Nathan, aphedwa kutsatila pakyombera komwe kunachitika, koma zigawengazi zinati sanali cholinga chenicheni chopha mayiwo anangokhala munthu wolakwika pamalo olakwika.
Izi zikutanthauza kuti zigawengazo zinkafuna munthu wina, koma zinatha kuwombera ndi kupha mayiyo mwangozi.

Khoti lalikulu la ku Western Cape linaweruza anthu awiriwa (Jeremiah Fortuin ndi Ricardo Cloete) chilango cha moyo wonse chifukwa cha kupha koopsa kumeneku

The Rez Nation TV πŸ“Ί.