Chitope herbal mixture
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chitope herbal mixture, Health/Beauty, Blantyre.
09/01/2024
Chitope herbal mixture amapangidwa kuchokera ku zinthu zodibwa zomwe zimapedzeka mma kitchen mwathu alibe side infect, tamuyesani lero ndipo simudzakhumudwa
09/01/2024
Amene tinapereka order juice Ali ready Tiyankhuleni pa ma number awa 0999782792/0888024760
Joice akhala ready Friday amene tikufuna tiyeni tipereke order, ngakhale zinthu zikukwerakwerabe mitengo koma ife a chitope herbal mixture mitengo yathu siidakwere ayi, mwina kumafunsa kuti ma hebal
Amenewa amachidza nthenda ziti, okay chitope herbal mixture amathana ndi matenda monga
Kuthamanga kwa magazi ( bp) chibayo, asthma, diebets, kuthentha kwa miyendo , mavuto
Zotumbq za mmimba, kupweteka kwa mmimba chifukwa cha period, amathandidzanso ku kwedza chitetezo mthupi , kungoyankhulako zochepa
, Ngati mutafuna m***a kutipedza pa ma number awa ' 0888024760/ 0999782
26/09/2022
Mankhwala akhala ready Wednesday, amene tikufuna tiyeni tipereke order, chifukwa ndimapanga kolingana ndi order yomwe ndalandira
Chitope herbal mixture, ndimankhwala omwe amathandidza matenda monga asthma,bp,, cervical cancer, amakwedzanso chitetezo chamthupi,zilonda zotsapora, amathandidza maso,kupweteka kwa mmimba chifukwa cha period,kuphwanya kwa miyendo komanso aphwesa mimba, kungokambako zochepa chabe, tipedzeni pa ma number awa kuti mumve zambiri 0888024760/0999782792
Chitope herbal mixture is now ready for more information call on 0888024760/0999782792
Juice ali ready amene tikufuna tipedzeni pa 0888024760 /0999782792 khalani athanzi nthawi zonse
Chitope herbal mixture is made from natural fruits and it helps people to have a good health for those that are HiV positive it helps to boost immunue system and also it helps to reduce high blood pressure, and it opens ovaries and many more if you want to know more about it you can call me or Whatsapp me on 0888024760
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre
BLANTYRE
