The world stories \kuphuzitsana
Knowledge is key to success
02/05/2023
DEFINITION OF LOVE 💞💞💞💞
Part 1 ~~
Ken anali mnyamata amene anakula mu umoyo wozunzika kwambir malingana ndimmene kwawo kunalili banja la kwa ken kunali nsikana mmodzi 🧕 amene anabadwa after 3boys oyamba anali ken ndipo wachili anali jama womalizila anali spata ken anali munthu amene amakonda kulemekeza makolo ake komanso ndi munthu aliyese samaona nkhope kapena kochokela kwa munthu. Kwawo kwa ken kunali kovutika kwambir malingana ndizoti panalibe munthu amene anaphuzila ndikufika form 4 pachifukwa chimenechi banja la kwa ken linali losowa muchuma ngakhale njinga yakapalasa 🚲 kunalibe choncho ken samaonesa Moyo wofuna kuwakhumudwisa makolo ake potengela ndimmene kunalili kukhomo kwawoko makolo ake a ken amakonda kulangiza ana awo kt akule ndimakhalidwe abwino choncho anawa amakhala omvela ndiso osatila malangizo amenewa akawalesa chinthu anawa samachipanga uwu unali Moyo wakwawo kwa ken
Ndeee tiyeni timve za nsikana uyu amene Zina lake ndi Tina 👩⚕️👩⚕️
Tina anali nsikana amene kwawo kunali kochita bwino chifukwa bambo ake amagwila ntchito m'boma pachifukwa Ichi sarary 💰💰 inali yochuluka mayi Ake a Tina anali munthu wa business zomwe zinapangisa kt banjali likhale la ulemelelo
Tina ankakanizidwa kupita out kukasewela chifukwa choti bambo ake anali aukali choncho amangokhala kumpanda konko tsiku lina makolo ake a Tina anali ndi ulendo wopita kumuzi kwawo ndipo Tina amayeneleka K*t akhale pakhomo zomwe zinapangisa kt Tina akhale wodandaula kt asala ndindan nanga azingokhala yekhayekha kumpandako posakhalisa makolo anachoka namapita kumudzi Tina anamusiyila chilichose chilipo sipanakhalise Tina anatuluka pa get pomunamiza mlonda kt akufuna akagule ndiwo zoti adyele masana km imeneyo inali plan yot akaone kunja basi ndipo mlonda anavomela Tina anatuluka km atatuluka anali ndi plan kt alowela kt poti mudzi sakuwuziwa bwinobwino kenako Tina anayamba kumangoziyendela basi
Pa tsiku limeneli ken anali atawona kt pakhomo lakwawo palibe ndiwo pomwe bambo ake an
26/04/2023
DEFINITION OF LOVE
💞💞💞💞
Nkhaniyi ndiyayifupi ndeee muyenela kuitsata bwinobwino chifukwa muli phuzilo lalikulu so ikhala ya fast tiyeni tipangeni follow page imeneyi kt chilichose tichimvele limozi
👇👇👇👇👇
DEFINITION OF LOVE 💞💞💞💞
KKKKKKKKK
09/02/2023
FIRST LOVE
Part 3
Nyasha ananyamuka kwa jama km ali okhumudwa malingana ndi mmene anayankhulila nzakeyi jama. Jama sanakhumudwe pachina chilichose sinanga amaziwa kt macheza ndi kulimba mtima basi choncho naye anangotenga zigubu namakatunga madzi kuchisime. Naye nyasha mmene amatulukila kwawo akuchita kukhala Ngt amamenyana ndeee waluza anangofikila kulowa kuchipinda kwake mpaka mlongo wake enifa anamudabwa kwambili nyashabanagona chasonga pabedi pake kuli kulingalila k*ti apanga bwanji k*t mkaxiyi atheke omuthandizila uja ndeee wakana ndeee zikhala bwanji. Kenako nyasha adalimba mtima basi k*ti naaa lelo lokha mkazi ameneyo afusila nyasha k*tada sanalimbaneso ndikudya nsima ayi anangolowa paline ndikumuhala Sasha mwamwayi amamupeza Sasha kt ali active kaya naye amagwila ntchito kwawoko timudabwe nanga every time online? Mkazi azitelo nanga. Keneko nyasha anayamba kucheza naye
Nyasha; zabho
Sasha; bhobho2 ka iwe
Nyasha; chimozmozi ase komano Sasha ineyo ndinali ndimawu amene ndakhala ndikulingalila k*ti ndikakuuza zindithela bwanji nanga iweyo uchilandila bwanji chimenechi ?
Sasha; mmmmmm zati bwanji lelo nyasha km OK ungathe kulankhula khala omasuka
Nyasha; thanks Sasha .ineyo nkhani yomwe ndilinayo ndiyak*ti kuyambila kale ineyo sindikumagona nawe tulo ndeee apapa ndafuna k*t ndisamangozisungila mumtimamu but ndikuyenela kulankhula basi ndeee if it possible k*ti ungatelo ndiuze.
Sasha; km nyasha kod mesa ndine mzako macheza ose aja akathele ukuku?
Nyasha; Sasha ineyo panalibe kuchitila mwina koma zomwe zinalipo ndizimenezi basi chonde Sasha.
Sasha; kd ndingakufuseko nyasha.
Nyasha; ungathe kufusa .
Sasha; iweyo ungandilonjeze chinthu chinachake?
Nyasha; eya ndizotheka ndipo ndine okonzeka.
Sasha; chabwino chomwe ndikufuna ine ndichak*ti iweyo undilonjeze kt suzandisiya komanso uzandichitila chilichose chimene ndingakulamule ndizokhazo basi.
Nyasha; I promise ndizakupangila chilichose chomwe unganene bola ungondilola basi.
Next
Timve mmene zinalil
04/02/2023
Nkhani idakalipobe chabe zinavuta ndizinthu zinazake basi mumaziwa kit ndife anthu ndeee something wrong
31/01/2023
FIRST LOVE
Part 2
Nyasha adasangalala kwambili atangowona photo yankazi uja mix anamuzindikila kit ndi sasha. Osaziwa k*ti sashayi ndichwanda chothela2
Ntahwi yomweyo macheza adayambika kungokhaka ngt anayamba kucheza kalekale km ayi kuyambila day imenneyo anthuwa adayamba kugona mochedwa amatha kufika 12:00 akuchezabe.week yachitatu nyasha adaganiza zoti amufusile mkaziyo km ayambila pati popeza nyasha anali munthu wowuma kufusila kunali chiphinjo kwa iyeyo km tonde nditonde basi anakumbukila k*t kuyenda awili simantha pompo adaganiza zokamufusa nzake jama mix akamupase plan yabho kt agwilebe basi. Nyasha ananyamuka Ku mmawa ulendo wakwa jama ndicholinga chak*ti akafuse zina ndizina nyasha atafika kwa jama adamupeza akumangaa mbuzi pamtengo anamudikila k*t amalize atamaliza anatengana tose wapantengo mkumakacheza kenako nyasha adayiyamba nkhani yake
Ase jama ndingakufuseko
Jama ; eya utha k*telo
Nyasha ; ase ndili nzanga koma ndinkazi mix ndikufuna nditamufusila koma poyambila pakusowa ndeee ndimafuna ndikufuse mix undipase ma plan.
Jama ; okay osadandaula ndik*thandiza ase ndiwe mzanga yekhayo km nkazi ameneyi ndiwak*t and ndindani?
Nyasha; Sasha wakwa mike
Jama ; mmmmm ase kkkkk usayelekeze nkazi ameneuja sangakukonde ndi chilombo
Nyasha; ase usayelekeze kundiuza zimenezo mkazi uja ndikumuziwa bhobho
Jama ; ndikhulupilile nyasha ndine nzako yekhayo ndingakuuze zabwino zokhazokha
Nyasha ; ndipo kwaleloli suli mbali yanga basi ndikupita kunyumba ndangotaya nthawi yanga
Jama; chabwino bola ndakuuza kenako nyasha anapita kwawo usiku utafika anafikila kulowa pa line k*ti ayiyambeno plan yofusila
Next part 3 tiwone k*t nyasha anapanga bwanji k*t agwile nkaziyo nanga zitheka?
# like and share
29/01/2023
Sorry azibale anga nkhani sitinaponye lelo chifukwa cha zovuta zina km mawa osadandaula FIRST LOVE ikubwela ndipo azibwela ma part ochulukilapo tiyeni tiyisate ndiyabwino
28/01/2023
FIRST LOVE
Part 1~
Ndinali ndili khale kwathu kusowa kt ndipite sipanathe 30minutes panatulukila nsikana wina yemwe dzina lake amamutcha Sasha.
Sasha: Nyasha ndamva k*t iweyo umaika WhatsApp mmaphone osiyanasiyana ndeee apapa ndabwela ndi phone yanga ikuvuta kuika WhatsApp ndeee ndimafuna undikonzele. Ine sindinalanyaze peza inali ntchito yanga komanso ndicholinga chak*t ndipeze ndalama mwina ndi ka holiday ka std 8 ndikamve bwino Sasha ndinamupasila phone yanga ndicholinga chak*ti ayigwile ine ndikumukonzela posakhalisa ndinamukonzela ndipo phone yake inakhalanano ndi WhatsApp kenako ndidamuuza kt andilpase ndalama yomwe ndamukonzela phone iye chimene adandiuza ndichak*ti:
Osadandaula nyasha ndalama yako ndikupasa komano silelo chifukwa ndilibe ndinazimvela chisoni kt ndangogwila ntchito yopanda malipilo komano osanama nkaziyo adali wowoneka bwino kwambili.
K*tada ndinadya chakudya chamazulo kenako ndinapita kuchipinda kwanga kukagona km ndisanagone ndinafuna kt ndicheze Kaye ndachibale pa WhatsApp. Nditasegula phone ndidawona Hi km nambala yachilendo ndipo imawonesa kt hy woyamba ndinapeleka ndine km sindmatha kukumbukila kt ndapelekela kt posafuna kundibalalisa tinacheza motele:
Macheza anyasha ndi Sasha :
Nyasha: ndani paja?
Sasha: ndine halima.
Nyasha: wakt?
Sasha : kubalaka
Nyasha unganditumizile photo yako mwina ndikuziwe ?
Sasha : OK
Kenako mkazi uja anatumiza photo ija km chodabwisa chinali chakt anajambulisa atayang'ana kumbali ndipo nyasha zinamubhowa kwambili kenako nyasha anati .
Ndakuona km sindikukuziwa ndeee utha kuipanga broke
Sasha : wandiona bwanji kumachita kt ndayang'ana kumbali
Nyasha zilibe ntchito bola ndawona chifukwa ndi mmene umafunila ukazafuan kucheza uzatumiza yowoneka bwino
Sasha :chacwino nditumiza ina
Nyasha : OK
Posakhalisa anatumiza km nyasha anazuma atawona kt ndimkazi uja Sasha
Wait part 2 timve kt zinatha bwanji pakati pa nyasha ndi Sasha
Osaiwala and share
27/01/2023
FIRST OF LOVE
Iyi ndinkhani yomwe ndiyophuzisa kwambili maka pa nkhani zachikondizi ndipo munkhanimu muli nyengo zosoyanasiyana zowawisa komanso zosangalatsa.
Ndee tikamawelenga nkhanizi tikhale tikuphuzilamo zina ndizina chifukwa nyengo zimenezi tikudusamo anthu ambiri .
Osaiwala kupanga AND SHARE k*ti nkhanizi zisakuphonyeni .
WE ARE GOING TO START OUR STORIES SO WE MUST TO LIKE AND SHARE ALL OF POSTS IN THIS PAGE OUR CREATER WILL BLESS YOU THANKS FAM
16/11/2022
David Livingston
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Machinjili
Blantyre
