Health tips

Health tips

Share

Wash up your body twice a day

Photos from Health tips's post 20/03/2026

*LONG LASTING MALE SPRAY*

aaaaaasa
Azibambo ambiriwa, or atatchena ambiriwa akukumana ndi vuto la eary ej*******on.
Eary ej*******on ikuchitika pa zifukwa zambiri
Kulera wa mayi,
Ma stress
Ma infections
Zakudya/zakumwa ndi zina Zambiri.

Nde ikakwana nthawi ya bwandulebwandule, kungogundisa nthawi yomwe malume fwaaaa.
Pamenepo mayi watetha ready kuti ayambe kuwakha ma penalty, bambo yambani, bambo ali ine ndamaliza kale.
Mayi akatero amangomezela mkhawa Ku mtima.
Izi zikamapitilira akudyerani ena muona ohhh.

Komano on a serious note vuto losachedwa kumathirali, azibambo ambiri nde akukumana nalo pa zifukwa zomwe ndanenazo. Nde kuti muthane ndi ma 20 seconds anuwo, yankho ndi male spray. Inu abale enatu or 1 minute samafika.
Male spray uyuyu umangomfaila Gadafiyo 20 mins before game. Zikatero uyo wadxuka kulilira ngati mkango. Nde umamugwila bwino ntchito mwana wayini ake kuti nayeso ayiwale njira ya kwawo. Aaaa osati kungoti gu nthawi yomwe fwaaaa.
Tagulani long lasting male spray

DESTINY HERBAL PRODUCTS
0885777241/0997088677

27/01/2026

Zizindikiro za mauka ni monga:
- *Kumva kuyabwa ku maliseche*
- *Kufiira kwa kumaliseche*
- *Kutuluka madzi kapena chikazi chochuluka komanso cha fungo*
- *Kumva kutentha komanso kupweteka kumaliseche*
- *Kumva ululu mkazi akangomaliza kugonana ndi mamuna olo kapena ululu akangomaliza kukodza*
- *Kutuluka tinsungu olo zilonda kumaliseche a mwamuna*

Zomwe zimayambisa mauka ni:
- *Bacteria or fungi*
- *Nyongolosi za mumatumbo*
- *Kuchepa kwa vitamin b nthupi*
- *Mankhwala (chemicals)*
- *Zopaka paka ndi kupopera mu pheche mpeche olo nthupi*
- *Kuvala zovala zothina kwambiri monga ma panti*
- *Kuvala zinthu zokuda komanso zonyowa monga mapanti*
- *Umve wa mkati*
- *Nthenda ya shuga komanso ma antibiotics*
- *Kusavala ma panti monga kwa inu adzimayi idzi zimapangisa kuti fumbi lidzilowa ku ndata kwanu*
- *Mankhwala ena*
- *Adzimai ena amatha kukhala ndi mauka chifukwa choti ngoyembekedzera*
- *Zakudya zomwe zili ndi shuga kwambiri*
- *Zokumwa zoledzeretsa*
- *Kugonana mosadzitetedza*

Ipa pali zipangizo zomwe zingakuthandizeni kupewa mauka:
🎯 Mukamaliza kugonana musavaleso pantπŸ‘™ unless maliseche muwonetsetse kuti awuma and mwatsuka.
🎯 Musamakonde kuvala zonyowa.
🎯 Musamavale pantπŸ‘™ mmodzi modzi.
🎯 Nthawi zina ma pant anu muzichapako ndimadzi otentha or muziyanika padzuwa osamangoyanika pamthuzi.
🎯 Ngati mulindivuto losachedwa kutuluka madzi kundata ngati mukuyenda muzivalira nyanda pant wanuπŸ‘™.
🎯 Mukamaliza kukodza muziwonetsetsa mwadzipuputa mikodzo yotsalirayo phuzilani kuyenda ndi tissue mu hand bagπŸ‘œyanu osamangodziwa kusungila face powder 🌝.
🎯 Mukamapita kosamba muzichapilatu pant ndikukayanika then kuvala wina osamasungila kuti mudzachape akada mapanti ambiri.

Mukusowa mtendere ndi mauka, bwerani ku inbox ya _DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS_ tili ndi mankhwala othetseratu matenda amenewa ndikuyambaso kukhara moyo wantendere osati omangodandaula ayi. Tipezeni kuno ku _DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS_ ngati muli kutali timatumiza ndipo mankhwala adzakupezani mosavuta 0885777241/0997088677.

Kuna ndani amene ali ndi swali kapena amafuna kuziwa zambiri pa mauka?

Photos from Health tips's post 20/11/2025

*UBWINO WA MA DELAY SPRAY*

Nkhaniyi tiyiyambe chonchi, Pali zithu zinazake nthawi zina munthu umatha kumazidusa chifukwa choti sukuziziwa bwinobwino, nde zikufunika kuti tiziziwa.
Azibambo Ena mphamvu zikutha mu tank ku chipinda, akumati akati akagone ndi mkazi or 1 minute osatha upeza akozera kale. Kuti abweleze kukanika go.
Ndiye ena amapeza makhwala ena akumwa, ngati achina Vi**ra, kamagra ndi zina. Ofcourse tiliso ndi ma herbs a man power, kuliso gondolosi kwapukwapu ndi zina.

Nowo izizi zakumwazi maka izizi za science muzapeza kuti ukazimwa zimabwelesa timavuto tingapo.
πŸ‘‰ Ena akamwa zimawapwetekesa mutu
πŸ‘‰ Ena amaona chizungulire
πŸ‘‰ Enaso amatha kukomoka nazo

Izizi zimachitika chifukwa choti, makhwala amene aja amathamangisa magazi, ndi chifukwa anthu amamva zoterezo. Nde kwa anthu omwe amadwala bp nde eeee samafunika kuti ayelekeze kumwa nawo ziachina blue pills ndi zina zija. Zimene zija zimapangisa kuti follow ya magazi ikhale fast kwambiri nde a ma bp inu mukhoza kuphulitsa nazo mavuto ena.

Fast forward tili ndi ma delay spray, awa ndi ma delay spray amene umawagwilitsa ntchito kunja. Magwilitsidwe ntchito ake umafaila chida chokha basi.
*Delay Spray amagwila ntchito bwanji*
πŸ‘‰ Ma delay spray awawa amapangisa Gaddafi uja kuti akhale olimba kotero amaletsa Kukozera mwachangu
πŸ‘‰ Amapangisa kuti chida chitote mwa mphamvu
πŸ‘‰ Amapangisa kuti mphamvu zibwele zoti ukamaliza uthe kupangaso.

*ubwino wina*
Ma delay spray alibe vuto loti uzimva ku wawa mutu, palibe zoti zikukomola mayazi.
Munthu yemwe amavutika ndi bp or sugar akhoza kugwilitsa ntchito bwino.
Izizi kumbali ya u moyo sizimaononga China chilichonse.
Alibeso vuto kwa mkazi.

Ife timakhala ndi ma delay spray ngati awa
πŸ‘‰ Long lasting Delay Spray
πŸ‘‰ Viga Delay Spray
πŸ‘‰ Maxman Timing spray
πŸ‘‰ Super dragon

Nde sikuti ndi ma spray okhawa enaso amakhala ma cream nde tili ndi achina Viga supermax cream, long er****on gel, nde ena kuliso ma delay oil. Ndi zina zambiri.

Kwa omwe mungawafune ma delay spray tili nawo ndipo tili ku Blantyre Ndirande market and Magalasi. Ife munthu akakhala ali kutali timatumizila.
Tilakhuleni mukazifuna.
Contacts:0885777241/0997088677
*DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS*

Photos from Health tips's post 11/11/2025

*LUMBRICINA OIL*

Azibambo nonse omwe mukumaziona kuti muli ndi chida chaching'ono or anakuuzani mwina madam kuti mukuchepa pamene pali sugar weniweni simukumapafikila. Eeee penatu akaziwa kulakhula kumawavuta sinanga amaopa kuti muwatenga ngati hule koma chilungamo chake ndithu alipo wena azibambo omwe or atakase bwanji koma penipeni pomwe pali sugar omupangisa kuti mkazi amve bwinopo iwowo samafikilapo.
Nthawi zina Gadaf akakhala wang'ono Pali Penapake ndithu pamavuta kupafikila. Komano musadandaule azibambo nonse omwe muli ndi ngini zing'onozing'ono tamvani za rumbricina oil uyuyu ndi makina dolo ka fafandede.
πŸ† Amakulitsa engeen ya abambo kuti iwonjezeleke ma inch mwamunayo akamachepa kuchipinda. Kukuza ukuku kuli pawiri Pali komapaka daily kuti ikuliletu nde kuti koti ungpfuna iwoneke yokula nthawi yokhayo basi. Koma mwa zonse akatunduwa amakuza chida cha abambo.
πŸ† Amathana ndi Kufooka kwa abambo kuchipinda. Nanga inu bambo otani omati akayamba kujiga engeen kuphwera panjira
πŸ† Amapangisa chida cha abambo kuti chitote mwa mphamvu, chida chikadzuka chizichita kuoneka mitsepha
πŸ† Kupangisa mwamuna kuti athe kubweleza
πŸ† Eyetu Gaddafi azitelera ndikutalika ngati m'lamba

Tili nayetu uyuyu wambirimbiri ku shop kwathu mitengo yake ndi yachibale basi mtengo pang'ono Gaddafi kukula thoo, m'kabudula muzimveka mndiiii.
Tili Ku Blantyre Kwa Magalasi komaso ku msika wa Ndirande ngati muli kutali timatumiza mukagula.
DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS
0885777241 /0997088677

Photos from Health tips's post 25/10/2025

TITAN GEL

Azibambo titan gel ndi cream mbambande amene amakuuza chida cha abambo.
Azibambo omwe muli ndi Gaddafi wang'ono ngati zikufunika Kukuza don't stress up.
➑️ Titan gel amakuza chida cha abambo ndi 3 to 5 cm mu mwenzi umozi
➑️ Amapangisa kuti upange improve magwilidwe a ntchito kuchipinda
➑️ Amapangisa chida chikhale cha mphamvu komaso chizitota nthawi yaitali ndi mwa mphamvu
➑️ Mwamuna yemwe wagwilitsa ntchito titan gel amakhala ready nthawi imene mkazi wafuna sangafere mu giya ayi.

Tili naye titan gel pa mtengo omvelera mthumba ndipo tikupezekela ku msika wa Ndirande ngati muli kutali timatumiza mukagula.
*DESTINY HERBAL AND BEAUTY PRODUCTS*
*0885777241/0997088677*

Photos from Health tips's post 22/09/2025

3 DAYS HIP & BIG BUTT

Ma capsules awa amabwelesa ma hip matako. Nyashi imachita kutuluka kawawa za amtsikana osamba izi, amtsikana oti Madzi aja samangophikila koma kusambaso.
Ma pills mbambande 3 days kuyamba kuona results.
♐ Kukuza matako
♐ Kukuza ma hip
♐ Makandamtchembere amachokaso
♐ Hormonal Enhacement

Mkazi aziziwika kuti uyu ndi mkazi akaima azipanga curve osati kungoti straight ngati mkhalamba ya ma 80'. Aaaaa Ladies mtengo pang'ono nyashi mbwembwe yospyesa mtima ija. Ngati banja likuvuta zitoleleni machick.

Tili ku Blantyre Ndirande kutali timatumiza
Tipezeni simuzakhumudwa.
Contacts: 0885777241/0997088677

Photos from Health tips's post 14/07/2025

ZOOMAX PLUS

azimayi uyu zoomax plus makhwala mbambande obweletsera matako ndi ma hip.
Makhwala opangidwa kuzipatso ndikuzitsamba omwe alibe chiospyezo chinachilichonse ku thupi lanu.

Matsiku anowo azimayi ndikuuzeni chinsinsi Cha azibambo, deal ndi chikhaliro ati khope azaona pamaliro. Nde chikhalirocho kuti chigwire bwino chinjanjepo bwino akaka ka zoomax plus.
Makhwala
1. Amabwelesa ma hip
2. Amabwelesa matako
3. Amanenepesa zonse thupi, kuti thupi lija lizifanana ndi thako labwera lija. Osati thako lino koma ka thupiko nde kang'onong'ono.
4. Zoomax amasalalisa khungu ukamwa zoomax sikuti nkhani ndi nyashi yokhayo ayi mumasalala. Amachitatu kumukongoletsa mkazi, kukongola ngati umasambira mkaka
5. Kwa omwe ali makandamtchembere/ma stretch marks ukamwa awa zimachokaso, osati nyashi yabwela makandamtchembere mbweee ayi.

Tili naye pa mtengo omvelera mthumba ndipo tikupezekela ku msika wa Ndirande and Magalasi kutali timatumiza pa courier ndi ma bus...
Contacts: 0885777241/0987474035

Photos from Health tips's post 21/05/2025

Discover the perfect skin care solutions at Destiny Beauty and Herbal Products! Visit our shop today and let us help you achieve radiant health and beauty. Your well-being is our Passion.
Contacts; 0885777241/0987474035

Photos from Health tips's post 02/05/2025

FAT BURNER

kuli anthu Ena omwe ndi onenepa koma kunenepa mopitilira, anapitiliza mulingo.ananenepesa. Inu kunenepatu nkwabwino koma kuliso ndi ma health issues ake kotero nenepani koma size yabwino. Nde kuliso Ena Ali ndi zimmimba. Basi mmimba khutchakhutcha aaaaa guys be serious.

Koma tili ndi fat burner uyu, amamphwesa thupi komaso kuphwesa mimba.
Ma girls kuphwesa mimba mukatchena kumaoneka ngati wa mmagazine.
Sizokhazo amalipanga refresh thupi makhwala awawa .
Komaso ndi body cleanser amachapa mthupi.
Inu muchedwelanji.
Tipezeni ife tili ku msika wa Ndirande ku Blantyre komaso kwa Magalasi 0885777241/0987474035

Photos from Health tips's post 17/04/2025

TALATIN 30

China mwa chomwe chimafotokoza kuti uyu ndi mkazi ndi hip. Atleast azimayi kumakhalako ndi hip .
Mkazi akaima kungoti see ngati paima pholo lamagetsi. Nde bolaso phaulo limakhala lamabumbump.

Ndiye product yomwe imabwelesa hip ina mwa Iwo ndi Talatin 30.
Uyuyu ndi matablet ndipo mkazi akamwa amachita kuumbika bwino Ka hip Ka bwino kaja kogwilika.
Nalo thupi limachita kutakasuka. Thako lizinjanja osati thako kungoti mphwathalala.

Nde talatin 30 tili naye ife pa mtengo omvelera.
Tili ku Blantyre Kwa magalasi ndipo anthu omwe muli kutali timatumiza.
Contacts: 0885777241/0987474035

Photos from Health tips's post 08/04/2025

IMMUNE BOOSTER TEA & ANTI VIRAL TEA

scientifically akatswiri anapezaso kuti tea ameneyu ndi tea wabwino amena amathandiza kubwenzeletsa chitetedzo mthupi. Chomwe ambiri sitizwa nchoti matenda ambiri amalowa mthupi akapeza kuti chitetedzo cha thupilo ndi chofooka ndi pamene, mthenda imamuonongera munthu.
Koma tea ameneyu amathandiza kubwenzeletsa chitetedzo. Osati kungobwezeletsa kokha koma mu nthawi yomwe ukudwalayo amathandiza.

Anthu amene mukudwala matenda osiyanasiyana makamaka matenda omwe atchukawo,ndibwino kupeza nthawi ndikumwa tea ameneyu. Amene muli ndi HIV bdi matenda ena. Tea amaneyu amakathandizila kupanga buld CD4 cells. Nkofunika kotani kuti tea ameneyu mukhale naye inu muzimwa kuti chitetedzo chanu chikhale pabwino.
Inu muli ndi HIv mutatenga tea ameneyu plus noni ndiye kuti eeee mwamanga linga labwino la yeriko pa mthanzi lanu.

Omufuna tea ameneyu tili naye pa mtengo omvelera.
Tili Ku Blantyre Kwa Magalasi ndipo kutali timakutumizilani.
WhatsApp or call 0884720023/0987474035/0885777241

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Nyamambadewe
Blantyre