Help me
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Help me, Health/Beauty, Nyambadwe, Blantyre.
Pano mitu siikugwira ayi. Akuyesela kuupukusa km opanda nyanga. Nkhani ndi mwana wa miyezi itatu. Akulira mosaneneka akayamba kulira akumakana chilichonse. Andifunsa ine chothandizo Cha momwe angamuthandizire mwanayo ndangowauza kt apite kuchipatala km akt apita koma sakupeza Vuto. Kupita kwa asing'anga sakupeza Vuto kumapemphero akumati akabwerako zikumayambikanso ndiye athandizeni a neighbor anga. Anzango omwe mukudziwa zochita please help me
Bambo a sikono polani moto
Kumwamba ndi kwabwino
08/10/2022
Uyu ndi *Sebastian Joseph* mnyamata wa zaka 13, yemwe wasankhidwila secondary ya boma ya Likuni Boys kuchokela pa Namachete Primary(Zomba). Kwawo ndi kovutikisisa amakhala ndi mai ake okha omwenso amadalila ulimi wokha. Tikupempha chithandizo kwa okufuna kwabwino k*t athandize chifukwa sangathe kulipila school. Aphunzitsi ake ayeselako kusonkha transport ndi kandalama koyambila koma nzosakwanila. Omwe angafune k*thandizapo atha kuimba pa 0992876139(mai ake) kapena 0884151637(deputy)
The most expensive liquid
in the world is a tear,
its 1% water and 99% feelings.
Think before you hurt someoneðŸ˜ðŸ˜ðŸ˜
Mkazi! chomuzunzira ndi chiyani ma boys?? ukuziwa k*ti sudzamukwatira, chomunamizira ndi chani, kumupatsa chiyembekezo mwana wa mwini wakeðŸ˜ðŸ˜ðŸ˜
Wakhala akukana amuna abwino kwambiri, kudalira iwe.
Wadikilira kwa nthawi yaitali k*ti uzamukwatira, lero uk*tengana ndi mkazi wina, why why & why?
CHIMODZIMODZI akazi mumapanganso mnkhalidwe umenewu, mamuna kukumphunzitsani bwinobwino, koma waipa lero chifukwa mwapeza masters degree, muk*ti si type yanuðŸ˜ðŸ˜ðŸ˜ ayi zikomo.
Kumupatsa chiyembekezo mwana wa weni, lero kumuthawa.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Nyambadwe
Blantyre
