The Wigs Factory

The Wigs Factory

Share

Malawi wigs!! Your confidence and your empowerment is our priority. �

Photos from The Wigs Factory's post 24/07/2026

Let’s vote. ☑️☑️☑️
Inu musankha waterwave utiyo? Picture 1 or 2?

23/07/2026

Ndavalatu wig ya ulemu, mukundiona kumeneko? Hehehe 😁😁😁 wig iyi ingakhale anthu ogwira ntchito yanji?
K60,000

21/07/2026

Tikamati Glueless full frontal wig, timathandauza kuti chani?

21/07/2026

M’ma komomu ka nyimbo aka bwanji? Ife ndiye kwathu kakumabvuta 😂😂😂
Glueless waterwave wig tavalayi iliposo.

20/07/2026

MWK 60,000 ONLY!!!

Kutchena kunatchipa tikutiii 😁😁😍

WOW! A nice ombre curly wig for you our beautiful customer, not only do you deserve the best😘😉😉😉 - koma kunena moopa Mulungu - WIG IYIYI?? 🥰 EEESSSHH

19/07/2026

New stock available this week kuno. We thank God for His faithfulness ♥️😊
If you’d like to see both new and old stock join our group 13 we post daily. 👇🏾
https://chat.whatsapp.com/HecrPwGiXLNKNu6SHajN1r?s=cl&p=i&mlu=4

19/07/2026

Inu lero muli mbali iti? Argentina ikawina, wig iyi ndikuchosela, instead of kugula pa K70,000 mugula pa K60,000. Discount poti tikhala tikusangalala. Ikaluza, ndichosela K5000 yokha. 😁😁😁⚽️⚽️⚽️

16/07/2026

Koma zowona?? 🥰

Chabwino World Cup yili apo, koma ma wig anu Ali motani? Zigoli zanu za ma wig ndi zigoli za Messi zikufanana? Taphatikiza nkhani inde koma nanga iyi yikuphonyeni? 🙊😁

Glueless frontal waterwave, I mean what could possibly be better?
K75,000 🥰

15/07/2026

Bwelani tisinthane, mundipase ma 10pin 6 okha, ine ndikupatseni wig iyi. Mukuona bwa?

13/07/2026

Abale ndithandizeni, a customer anabwela kuzagula wig iyi, ndawuza ma wig ali pa 75,000 imodzi, ati ayi iwo ali ndi K40,000. Ndipo ndingoyenera ndiwachotsere. Akuti sachoka mu shop mwathu mpaka ndiwachosele. 🙊

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Blantyre

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 17:00