HerbBank Mw
The home of organic herbs/food supplements(international standards) Lilongwe & Limbe
We provide free natural healing guidelines and sell herbs and food supplements
09/05/2026
Mankhwala opaka a njerewere zapakhungu k10000 each, tea wothana ndi matenda achiwindi, obereketsa komaso amavuto ammimba k20000 aliyense,yoni detox pearls k4000,LILONGWE & LIMBE kulikonse timatumiza 0994726617
18/02/2026
*TONGKAT ALI TABLETS*
K35, 000 only
*Results are instant*
Awa ndima tablets apamwamba kwambir omwe muli tongkat ali, Shirajit,maca ndima herbs ena.Tongkat ali amathandiza zinthu izi kwazibambo;
1. kupanga boost ma hormones monga testosterone level
2. Kupeleka chilakolako chogonana (boosts libido) pochulukisa umuna kukhala wokhatamira
3. K*thandiza abambo kupeleka pakati (boosts fertility)
4. Kupeleka nyonga (energy booster)
5. Kuchepesa bvuto la Kuchuluka Kwa sugar mmagazi (Diabetes)
6. K*thandiza mzeru (boosts memory)
7. K*thandiza abambo kutota Mwa mphamvu (corrects erectile dysfunction)
8. (Fights free radicals )kuthana ndi madzi oyipa mthupi
9. Kuchotsa nkhawa(stress)
Note: zosatira ndi same day
WhatsApp/Call on 0881495971
18/02/2026
*VITILIGO REMOVAL CREAM*
K15,000 only
Vitiligo ndimatenda omwe khungu limawoneka ngat lachalubino.
Izi zimachitika pomwe ma cells akhungu akulephera kutulusa *melanin* okwanira pamalo ena.
Vitiligo cream amawapanga ma cells kuti ayambenso kutusa *melanin* okwanira ndikuchotsa ma *white* *patches* pa khungu
Mtengo ndi k15,000
Mukagula muzawuzidwa Kagwiritsidwe ntchito kake
Alipo kumashop athu ku Lilongwe ndiku limbe
18/02/2026
*MACA ENERGY TEA*
K30,000 Only
Uyu ndi tea wa aliyense kupatula ana yemwe ntchito zake ndi;
1. Boosts libido (Kupeleka chilakolako chogonana)
2. Tonifying kidney (K*tsuka ipso)
3. Improves s***m motility
4. Hard er****on (kudzutsa mwandi)
5. Long lasting(kukhalitsa pamwamba)
6. Stimulates men potential
7. Improves Immunity (Kuwonjezera chitetezo)
8. Treats Insomnia (Kusowa tulo)
9. Balances hormones
WhatsApp on 0881495971
17/02/2026
*YONI DETOX PEARLS NDICHANI?*
Awa ndimankhwala achilengedwe opangidwa kuchokela ku zisamba omwe amathana ndimavuto aliwonse okhuza njira ya Chibelekero cha amayi (Gynecological problems) ndipo ena mwa mavuto omwe Yoni Detox Pearls amathana nawo ndi;
1.zotupa zamuchiberekero
2.kukanika kutenga pakati
3.akatenga pakati pakumachoka
4.mauka
5.kutulutsa chikazi chotsakhala bwino chonunkha
6. fungo lakundata
7. kukula kwa ndata
8 nthenda ya munjira yamkozo/ UTI
9. kusekeka kwa chibelekero
10. endometriosis
11.ululu pogona ndi mwamuna
12.ululu nthawi yosamba (cramps)
13. kusamba kosaleka
14 komanso kusasamba kumene.
Yoni detox pearls amayamwa zonyasa zonse zamuchiberekero komanso kundata kuzitulutsa kunja, kuphwetsa zotupa zonse, zoonongeka zonse kuzikonza mpaka mafungo onse kutha mayi kukhala ndi muchiberekero mokonzeka bwino kutenga pakati mbali inayi ndata kuisiya yochepa yothina bwino.
Helpline:0881495971
K4,000 each
16/02/2026
*C-4 MANKHWALA ONENEPETSA
C-4 K22,000
Mayi, Bambo kapena mwana mukufuna kunenepa?
Tili ndi mankhwala opangidwa kuchokera ku zipatso a *C-4*
*Ubwino wa C-4*
ali ndi ubwino uwu;👇
1. Kunenpetsa thupi momwe munthu ukufunira.
2. Amathandiza ana onyentchere kunenepa komanso kukula
Mankhwala a C-4 amagwiritsidwa ntchito ndi winaaliyense *Bambo, Mayi* komanso *ana*
Mankhwalawa amathandiza ndi odalirika 💯 ndipo zotsatila zake zimayamba in 2 weeks
WhatsApp 088149597
12/02/2026
K*theka K*t mzanu Ali ndi vuto la vitiligo (kukhala ndi ma pach oyera pakhungu) koma sakudziwa K*t mankhwala Ake tili nawo mk13000
10/01/2026
K*theka K*t mzanu Ali ndi vuto la vitiligo (kukhala ndi ma pach oyera pakhungu) koma sakudziwa K*t mankhwala Ake tili nawo mk13000
27/11/2025
KUTI MUBEREKE
PAKUFUNIKA MAYI NDI MZIBAMBO AKHALE NDI CHONDE NGATI PALIBE CHONDE TENGANI MA HERBS OPATSA MPHAVU NDI CHONDE FERTILITY mumafuna thandizo tipezeni Lilongwe ndi Limbe or call 0994726617
20/05/2025
LILONGWE SHOP; GATE LOLOWERA MA BUS AKULU (LILONGWE BUS DEPOT) OSALOWA KWEZEKANI PANG'ONO KU LEFT SHOP # 44
LIMBE PACIFIC TOWER SHOP /2.
Tili ndi ma herbs othana ndi mabvuto ambiri 1.body boost(hips/butts),
2.weight gain(male& female)
3.slimming/flat tummy
4.skin and toothcare
5.detox and immune booster
6.libido, fertility,sexual energy& other health problems
Helpline: 0994726617/0881495971
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Limbe
Blantyre
Opening Hours
| Monday | 09:00 - 17:00 |
| Tuesday | 09:00 - 17:00 |
| Wednesday | 09:00 - 17:00 |
| Thursday | 09:00 - 17:00 |
| Friday | 09:00 - 17:00 |
| Saturday | 09:00 - 17:00 |
| Sunday | 09:00 - 12:00 |
