Madzi Nkalo official

Madzi Nkalo official

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Madzi Nkalo official, Health/Beauty, Blantyre.

24/01/2024

AFTER HEARTBREAK
AGOGO :bwanji ukuzungulira nyumba, ukufuna chan?πŸ€”
ME :Simungazimvesetse ndinu ana πŸ˜§πŸ˜…πŸ˜‚πŸ€£πŸ€£

24/01/2024

AFTER HEARTBREAK
AGOGO :bwanji ukuzungulira nyumba, ukufuna chan?πŸ€”
ME :Simungazimvesetse ndinu ana πŸ˜§πŸ˜…πŸ˜‚πŸ€£πŸ€£πŸ™Œ

31/12/2023

Me(pa 31 Dec)::lero nde tigona panjatu😜

Nsikidzi::mawa limafika😏

04/11/2023

Ma boys nd ma girls akati anameπŸ—£
"Mzakukonda mpaka dzuwa lidzathe ma battery"πŸ™„πŸ˜…πŸ˜ŽπŸ’”πŸ˜†πŸ€£πŸ₯°πŸ™ŒπŸšΆ

03/10/2023

Jacama Kumwembe against Extreme FC. His attempt went off target. Uyu apweteka matimu πŸ˜…

03/10/2023

ZINTHU 10 ZOWONA KOMA ZOTSEKETSA 🀣🀣🀣

1:Sungasuke maso ako ndi soap
2:Sungawerenge tsitsi lako
3:Sungathe kupumira mphuno pomwe watulutsa lilime lako
4:Apa wayesera kupanga No: 3
6:Pamene wapanga No :3 waona k*t mzotheka kupuma bwino bwino koma ukuoneka ngati galu🐢🐢🐢
7:Ukumwetulira panopa chifukwa wapusisidwa
8:Sunawerenge number 5
9:Wasakasaka k*ti uone ngati palidi number 5
10:Wamwetulira poona k*t number 5 palibe

Hahahahahaha muzikhala srs
🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Blantyre