Remedies for life

Remedies for life

Share

-Learn to be your own doctor and save money

04/12/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rowland Gladson Chatonda Munthali, Henry Mukhuna, Bornface Djmarenz Maeresa, Besta Matayah Chifundo, Billy Dennis, Donald Mchombo, Nelson Liwonde, Emily Nyakaphika Nyirongo, Gabriel Chelwa, Wallusungu Mphatso Kallua, Oyimbo Baxter Manase, Joseph Titus Majinga, Dominic Munembo, Brunno WA Steven, Møtrick James Vîvîlâ Sákåh, Frank Shook San, Maneno Musambara, Alex Msowoya, Triple Kay Khobwez, Ramsey Kamwana, Sidala Gidala, Dan Matola, Blessings Kaamba, Frecious Mlauzi Nkhoma, Atusaye Silumbu, Steven Austine Dagama, Tryness Gondwe, Martias Mtima, Moffat Chimbwala, Chancy Zuma Nyirenda, Esther Keyz Namaseko, Gerald Kamphinda, Siliya Kay Piason, Noel Linde, Peter Limbe, Martha Selison, Smith Mwanza, Felister Jawaduh Bamusi, Clesencio Lyton, Andy Andrew Willie, Beatrice Kamkwamba, Moffat Njiwa, Lick-cess Mwaleh, Walter Ndhlovu Loughton, Bridget L.M. Banda, Ali Dickson, Bright Solomon, Mercy Frank, Eric Youlic Haïti Bonja, Mphaso Chisale

02/12/2025

*MWANA MPHEPO*

🎯Mwana phepo ndimatenda omwe amatha kupanga mimba kapena panja pathupi,_

🎯Mwana phepo alipo mitundu iwiri Pali mwana phepo wa mimba komaso wapanja pathupi.

🎯Kodi mwana phepo ndichani mwana phepo ndi zilonda zomwe zimakhala mimba komaso panja.

🎯Mwana phepo amatha kubwelesa vuto lakusabeleka komaso sagwira amayi okha ayi or even abambo

Nthawi zambiri ukamadwala mwana phepo mimba mumangolira

SANKHANIPO REMEDY IMODZI APA `
(Treatment)
1️⃣🌈 ` Pezani zitheba za moringa chamwamba muziwirise muzimwa katatu pasiku.

2️⃣🌈 Pezani mtengo wama huhu masamba akewo kwawirisa kumamwa kawiri pasiku.

3️⃣🌈 Pezani misitsi yama sache aja mumasesela panja aja akunchire,,, muwirise kumamwa katatu pasiku,

4️⃣🌈 pezani masamba achitimbe muwirise kumamwa katatu pasiku.

NANGATI NDI CHILONDA
🎯Pezani makala mix turmeric powder kusnjira limozi komaso masamba amatowo or amango nde muzimatamo mabalamo

Remedies for life WhatsApp group 0993966501/0885038351

13/06/2025

*BRUSH TREE*

🌽☆Brush tree ndiwabwino mnjra zambiri ndipo ndi remedy yokhayo yomwe payokha imachita ma miracles.

🌽☆Brush tree imaonjezera chitetezo kwa anthu omwe ali HIV POSITIVE.

🌽☆Brush tree amathandizanso ku vuto la *BP* moti ngati muli ndi vuto la BP yesani brush tree.

🌽☆Brush tree amathandizanso vuto la ma *fibroids* ndipo ndi wachangu kwambiri.

🌽☆Brush tree *imapoletsa zilonda za cancer* ,kwa inu amene muli ndi zilonda kapena wachibale. Bwatitsani zikhatho ziwiri za brush tree ndi madzi okwanira 1 little ndi kumatsukila chilondacho ndipo chimachila mwa msanga.

🌽☆Brush tree *amapozaso zilonda zosapola* monga za matsenga ,kapena zakumidima.

☆Brush tree amathandiza popanga *neutralise poison* pamene munthu wamwa kapena kudya chakudya cha poison. Imwani brush tree tea.

🌽☆Tsilani madzi a brush tree, *pachilonda* chomwe mwangovulala kumene ndipo ululu umasowa ziii.

*Brush tree ndi mtengo omwe ambiri timadzala ngati maluwa 🌹ndipo umakhala ndi maluwa onga brush, ofiira ndi timasamba take ting'onoting'onoting'onoting'ono
Umakhala ndi nthambi zokula mowelamilamowelamilapasi

13/06/2025

Big shout out to my newest top fans! Provi Matsimbe, Thoko WA Ellen Alecho, Henderson Kapusa, Beatso Kay Umali, Prisca K Banda, Lovely Daniel, Chirwa Zondie, Maria Manda, Joice Nyakhonde, Fishani Nyirongo, Marie Mwimz, Chisomo Lastborn Angozo Marko, Dyson Pondani, Macsozi Magudanya, Alinafe Chandiyang'ana, Matrida Gavern, Akuzke Malemia, Loyce Folotia, Çhichi Phiri, Pra Ise, Mwenekabwe Kayondo Silumbu, Frank Malota Jnr, Irene Kondowe, Loveness Joseph, Inkosi Hosea Mbewe, Mzatiwathu James, Shirrah Kamoto

10/06/2025

*"VUTO LA KUDZIMBIDWA / CONSTIPATION"*

👉 Kudzimbidwa ndivuto lokhudza kayendedye komaso kagayidwe ka zakudya m'mimbamu

*ZIDZINDIKIRO ZAMUNTHU YEMWE WADZIMBIDWA*

👉 Munthu yemwe ali ndi vuto lakudzimbidwa amaona zinthu ngati izi.

👇👇👇👇👇👇👇👇

👉 Kufufuma kwa mimba yake
👉 Kuphwisa pafupipafupi
👉 Kugeya pafupipafupi
👉 Kupita ku toilet kuti akaBiBe koma amangokatsitsako mpweya mkubwelerako.
👉 Kutulutsa BiBi yolimba koma ili yochepa
👉 Kuva kupweteka kwam'mimba.
👉 Kumva kunyong'onyeka m'ma joints pena ngati angotapambalala asagwile ntchito.
👉 Kufooka mayang'anidwe komaso kufooka kwathupi

👉 Ngati vutoli lakhalitsa osachizika kapena ngati akudwala pafupipafupi vutoli, munthuyo amatha kuyamba kudwala matenda a likango lakoBiBila, Vuto lakuva kuyabwa koBiBila limayambaso ndi kudzimbidwa, osayiwalaso kuva kupweteka koBiBilaku komaso kutulutsa BiBi yamagazi nthawi zina ndi chifukwa chakudzimbidwa pafupipafupi kapena kwa nthawi yayitali.

*NJIRA ZACHILENGEDWE ZOTHANIRANA NDI VUTO LA KUDZIMBIDWA*

*1). UNFILTERED APPLE CIDER VINEGAR."*
👉 Apple cider vinegar amathandizira kwambiri pakayendedwe komaso kagayidwe ka zakudya m'mimbamu.
👉 Tengani ma tiyisipuni atatu a Apple cider vinegar kuyika mu tambula yoti muli madzi mkusungula nde muzimwa pang'ono pang'ono kuchoka m'mawa mpaka masana.
👉 Madzulo wa mupangeso chimodzimodzi ndi tambula ina mutathiramo ma tiyisipuni atatu mkumamwa pang'ono pang'ono ngati simukufuna mpaka mutamaliza.

*2). OLIVE OIL"*
👉 Olive Oil amathandizira kufewetsa zakudya zomwe zikulephela kugayika bwino m'mimbamu.
👉 Imwani ma tebulosipuni awiri a Olive Oil m'mamawa musanadye kalikonse .
👉 Komano musamwe matebulosipuni opitilira atatu a Olive Oil pakamodzi chifukwa zikhoza kuyambitsa vuto lakutsekula m'mimba. Komaso musamwe kwa nthawi yayitali Olive Oil.
👉 Olive Oil amachepetseso mulingo wa sugar m'thupi

*3). UCHI WA NJUCHI"*
👉 Uchi nawo umathandizira kufewetsa zakudya zomwe zikulephela kugayika bwino m'mimbamu.

Remedies for Life

10/06/2025

*_TIYENI TIONE MAVUTO OMWE AMADZA KAMBA KA KUKWERA KWA NTHENDA YA SUGAR_*

✍️ *MAVUTO A MASO.*
Pomwe sugar yachuluka imapanga affect mitsepha yomwe imapita Ku maso zotsatila zake umavutika kuti uwone.

✍️ *MAVUTO A UBONGO.*
Sugar akakwela imaononga mitsepha ya Ku ubongo ndi chifukwa chake its easy munthu wa sugar kupanga stroke.

✍️ *IPSO NDI CHIKHODZODZO.*
Pomwe muli sugar zimapangitsa kuti ipso yanu izikhala ndi tchito yochuluka zomwe zimapangitsa ipso yanu kuonongeka.

✍️ *HEART ATTACK*
Sugar akachuluka amapangitsa kuti mukhale pa chiopsezo chodwala nthenda ya mtima komaso angina.

✍️ *ZANZI ndi MABALA*
Sugar ikakhala yokwela munthu amamva dzazi,penaso kutuluka bala lomwe limavuta kupola komaso siliwawa tamvako anthu akudulidwa chiwala chifukwa cha sugar.

*Chimachitika kweni kweni ndi chani ndi nthenda ya sugar?*

Sugar akachuluka nthupi zambili zimasitha monga kuotcha kwa mapazi,dzazi,kutuluka zilonda,izi zili chocho chifukwa choti sugar ikachuluka imaononga zedi mitsepha.end result ndizilonda zokanika kupola,dzazi,mapazi kuotcha.

*Tingatsate njira ziti kuti tidziwe msanga mvutoli*

👉pangani check kumapazi kwanu ngati kwatuluka kachilonda komwe sikakuwawa mukakapeza visit doctor.

👉ngati mwapezeka ndi sugar mwatuluka nthuza,njelewele musafidye/kudula nokha uzani doctor.

*Natural remedies for sugar*

👉Muzimwa tea wa mandimu tsiku ndi tsiku

👉Muzitafuna adyo mutatu a day kumwela madzi tambula limodzi

👉Wilitsani madzi amasamba agwafa or mango 1lt muzionetsetsa kuti 1lt yonse mwamwa tsiku lonse

👉Muzikonda kudya maungu

👉Pewani kumwa ma soft drinks omwe muli acid

👉Pewani kumwa madzi a fridge

👉Idyani nkholowa pafupi pafupi

👉Tichepetse kudya za sugar zedi ndi mchere.

*Pomaliza onetsetsani madyedwe anu muzidya zakudya zambili za masamba,ma natural fruits,pewani kumw
a mowa zedi,kusuta fodya,pewani kudya zakudya za sugar zedi*

Remedies for life WhatsApp group 0993966501

10/06/2025

*ZIZINDIKIRO ZAKUTI IMPSO YANU ILI NDIMATENDA.*

*SYMPTOMS OF KIDNEY DISEASES.*

*01.👉.* Kukhala otopa komaso opanda mphavu .
*02 👉.* Kuvutika kuti mupeze tulo.
*03.👉.* Kuuma kwa khungu komaso kuva kuyabwa pakhungu.
*04.👉.* Kukodza pafupipafupi
*05.👉.* Kukodza mophatikiza ndi magazi.
*06.👉.* Kukodza mkodzo wathovu.
*07.👉.* Mavuto ena a maso amabwera chifukwa cha mavuto a ipso.
*08.👉.* Kutupa kwa kasukusuku (Ankles) komaso mapazi.
*09.👉.* Chilakolako cha chakudya chimachepa.
*10.👉.* Kupweteka kwama muscles.

*NJIRA ZA CHILENGEDWE ZOTHANIRANA NDI MAVUTO A IMPSO*
👉 Pezani nthanga za chibvende🍉 muzisinje mupange ufa muzithira mu tea/phala.
👉 Nthangala za Maungu muziziyanike zipange ufa, muzithira mu tiyi muzimwa.
👉 Pewani mkaka wang'ombe komanso zakudya zochoka ku mkakawu.
👉 Nyenje za chimanga ndizamphamvunso kwambiri pothana ndi vutoli.
– Muziwilitse ndikumamwa, kenako kumathowa mbari ikupwetekayo ndi madzi otentha othiramo jinja.
👉 Muzima madzi ofinyidwa m'mandimu komanso ma juice azipatso zosiyanasiyana .
👉 Mupewe shuga ndi nyama zonse ndi zoipa kumbari ya thanzi lanu makamaka ku impso.

Remedies for life Whatsap group 0993966501

10/06/2025

*LOW BLOOD PRESSURE KOMANSO KUSOWA KWA MAGAZI / ANAEMIA*

Kuchepa kwa magazi m'thupi kumayambika kamba ka zifukwa zosiyanasiyana monga kusadya zakudya zamagulu, cancer, malungo ndimatenda ena.

*ZIZINDIKIRO ZA KUCHEPA KWAMAGAZI M'THUPI"*

👉 Kukhala ndi ulesi nthawi zambiri,
👉 Kukhala otopa nthawi zambiri.
👉 Maso kuoneka oyera kwambiri.
👉 Namo m'manja mumakhala moyera.
👉 Kupanga chizungulire pafupipafupi komanso kusowekera mphavu yamayendedwe (Balance )
👉 Kupweteka kwa mutu pafupipafupi.

*NJIRA ZA CHILENGEDWE ZOTHANIRANA NDI VUTOLI*
👉 Teaspoon imodzi ya blackstrap molasses mu madzi okwanira 200ml, kumwa m'mawa ndi madzulo
👉 Muzidya kwambiri salad wamasamba a green, masamba a green amakhala ndi chlorophyll yemwe akalowa m'thupi amasanduka haemoglobin ndipo magazi amabwerera mwachangu ndikuyamba kuyenda bwino.
👉 Teaspoon ya ufa wa Moringa (Cham'mwamba) kuthira muphala katatu patsiku, mudzachira nsanga.
👉 Muzidya zipatso zambiri maka pa breakfast ndi nthawi iliyonse.
👉 Muziwiritsa chidede chokwanira chikhatho chimodzi mu madzi okwanira litala imodzi ndipo mugawe patatu ndikumwa katatu patsiku osathiramo kalikonse.
👉 Mupeze jinja wamkulu bwino wamuwisi 4, munyenyeni ndipo muwiritse mu litala imodzi ya madzi ndipo muzimwa musanadye kanthu.
*Komano.* Jinja asamwe munthu wamimba kapena oti akudwala matenda ena, amatha kukweza bp.
👉 Mukakhala ndi low blood pressure muzidya mchere wambiri, sodium amapangitsa kuti magazi ayambepo kuthamanga.
👉 Musiyiretu kumwa mowa chifukwa mowa umatsitsiratu kayendedwe kamagazi nde vutoli limakula.
👉 Kukhala mopana miyendo kumakweza bp, wa bp yokwera sayenera kupana miyendo akakhala, koma kwa wa low blood pressure, njirayi imathandizira kukweza bp.
👉 Kumwa madzi pafupipafupi kumathandiza kuchulutsa magazi speed yake, ndipo moteromo mumapangisa kuti low blood pressure uchire.
👉 Muzidya zakudya zochepa koma pafupipafupi, izinso zimathandiza kukweza kayendedwe kamagazi.

Remedies for life WhatsApp group 0993966501

10/06/2025

KHASA YA MALISECHE AMAMUNA(PINALE CANCER)

Mbuyomu tinakambilanapo Kuti khasa ilibe malo eni eni pathupi lamunthu`

ZIZINDIKILO ZA KHANSA

1️⃣Kukodza pafupi pafupi

2️⃣Kukodza movutikira

3️⃣Mphavu zakuchipinda kuchepa

4️⃣Gaddafi kulephera kudzuka

5️⃣Kuva kupweteka pogonana

6️⃣Kutuluka magazi pokodza mophatikiza ndi mafinya

7️⃣Kuwawa musi mwachiuno

⚠️Mukazadabwa zizindikiro izo zikukuchitkirani pafupi pafupi thamangirani kuchipatala Kuti mukayezetse khasa yamaliseche anu.

TREATMENT YAKE

1️⃣OMEGA 3 FISH OIL
Mudzimwa tablet ma tablet awili tsiku lililonse kwa masiku okwanira 90 ndipo mudzachiriratu ku cancer ili yonse.
Muzimwa juice wa carrots🥕 every day

2️⃣Nyenje zachimanga kuziwilitsa madzi akewo kumamwa within 24 hours

3️⃣Nthangala zamaungu zouma muziwiritse madzi akewo half cup kumamwa every day

4️⃣Muzipasa odwalayo madzi otetha amandimu every day

5️⃣Muzidya kwambiri adyo or anyezi

6️⃣Ngati Pali chilonda tengani black seed oil, uchi, ginger kumapakapo muzachira.

SANKHANI REMEDY IMODZI PA NTHAWI IMODZISO

Heaalty Herbal Clinic timanena kuti odwala ndi amene amafuna doctor timadziwa kuti kwa anthu omwe zomwe taponyazo sizikuwakhudza akamawelenga amawona ngati zikungowadyela nthawi, koma kwa amene ali ndi vuto tikaponya remedie yogwilizana ndi vuto lawo amakhazikikapo ndikupindulapo.

Remedies for life WhatsApp group 0993966501

10/06/2025

*NEEM/MKINA*

∆ Nimu ndi cholengedwa chomwe chimawawa kwambiri, mtengowo umatha kutenga masamba kupanga powder ( ufa) , ma tablet, ma capsules ndi mafuta ( oil)

-Nimu umachiza pafupifupi nthenda ina iliyonse kupatula *imfa*

*NJIRA ZACHILENGEDWE*

~Mukamakonda kumwa Neem simuzakhala pa chiophyezo chodwala matenda a Cancer.

~Ngati mwatenga matenda opasirana kudzela kugonana musachedwe, imwani Neem akuthandizani mwansanga.

~Kuti muthane ndi kudzimbidwa komanso kukula mimba mupeze Neem muzimwa.

~Kwa amene mukuvutika ndi matenda a mtima pezani Neem.

~Ngati simuchedwa kudwala malungo kapena mumangomva kudzidzira nthawi zambiri muzimwa Neem.

~Mukhoza kugwirisa ntchito Neem ngati emergency pill kuti musatenge mimba 🤰🏽mukamariza kumenya game.

~Neem amathandiza kutsitsa sugar wa mthupi mwanu ngati akukwela(Diabetes).

~Ngati mumavutika ndi matenda a mu usinini mupeze Neem.

~Mukhoza kugwirisa ntchito Neem ngati mukufuna kutsuka mthupi.

~Inu amene mukuvutika ndi mfundu za mmutu mupeze Neem akuthandizani.

~Kwa amene muli ndi matenda a mu Liver muzikonda kumwa Neem.

~Neem amathandiza kuthana ndi ma fungus.

~Neem amathandiza kuonjezera chitetezo cha mthupi. 🙉

~Kwa amene mukuvutika ndi ziphuphu kumaso pezani Neem mudzipaka kapen kumwa.

~Kwa amene mumamveka mafungo anthupi muzisamba madzi othira neem

~Kwa amene alindi mfundu mmutu kupeza masambawa kusinja kuwilitsa madziwo Kutsukira mmutu

~Kwa amene akumva kuyabwa mthupi or mwatuluka anabiri or zidzolo pezani masamba amenewa wilitsani ndikusamba madzi amenewo.

~ Omwe muli ndi vuto la HIV pezani Nimu.Muzimwa

_Nimu amachiza matenda ochuluka ena sindinawalembe pano, onetsetsani kuti mnyumba mwanu muli ndi Nimu_

06/06/2025

1 day skin challenge! ALL DARKSPOT IS GONE..

TAPEZANI CLOVE POWDER NDI ALOEVERA

TENGANI ZANKATI MWA ALOEVERA ( ALOEVERA GEL) MUSAKANIZE NDI POWDER WA CLOVE.

KAGWILITSIDWE KAKE

TENGANI ZOMWE MWAPANGA ZIJA (ALOEVERA NDI CLOVE POWDER) PAKANI PAMENE PALI VUTOPO MUKHARE NGATI MUKUTIKITIRAPO KENAKO DIKIRANI KWA 10-15 MINUTS,

LETS SEE IF YOU WILL STILL HAVE SUNBURN AND DARKSPOT AGAIN...

REMEDIED FOR LIFE WHATSAP GROUP 0993966501 JOIN OUR WHATSAP GROUP AND LEARN MORE

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe Area 14?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Lilongwe Area 14

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Sunday 09:00 - 17:00