Nekhantan onekha

Nekhantan onekha

Share

Ngat kucheza mumatha tiyen TICHEZE tiseke basi �����

26/12/2024

Kumakhala ngati kachinyama aka. Ak*ti dzina lake ndi axolotls.
Family ya tizinyama ngati achule.

Ati ali ndi smile ya permanent.

Kumangomwetulira basi 🤭

Ak*ti tinastalapo tochepa pa dziko lapansi.

Photos from Nekhantan onekha's post 01/09/2024
22/07/2024

Uyu ndi makechulu
Video iyi ikuwonetsa momwe make chulu amaikilila mazila omwe akasweka kumabadwa ngumbi komaso chiswe

Chiswe chimakhala chikukoza njila kapena k*ti timayenje timene ngumbi zikabadwa ndi kukula zimadzadutsamo pamene zikufuna kukawuluka

Komaso make chulu amadyetseledwa ndi chiswe chomwe chimakhala chik*tetezela makechuluyoso

Make chulu amaikila tsiku lililose mowilikiza
Komaso chiswe chimakhala chikupanga masachi makechulu k*t thupilake lizitha kukhala logwila bwino tchito yake

Next k*ti tipitilize
-onekha

08/07/2024

Iyi ndi ng'ombe yammadzi yomwe yapezeka kumaiko azathu akunja

Asodzi omwe amakokolola somba ndi kombe ndi omwe akokolola somba imeneyi

Kom zikudabwitsa kwambili chifukwa ndikoyamba kupezeka somba ng'ombe ..

-onekha next k*ti tipitilize komaso k*t tidziwe ndikuphuzitsana zambili..

18/06/2024

UTHENGA UWU
NDATUMIZA KOMA
NDILI OTHODWA

inu mudamukonda koma ambuye amukondetsetsa

Valani Chovala chilichose km Mulungu ndy chovala chanu chomaliza,

Yendan m'mene mungayendele km IMFA ndy Ulendo wanu omaliza

, Kwelani Njinga, Galimoto, Ndege ndizina zonse Km BOKOSI ndy Chokwela chanu chomaliza

pitan maiko otchukaw kma kumanda ndilo dziko lomaliz

gonan muzinyumba zokongolazo kma mudzenje ndyo nyumba yanu yomaliz

Maina anu angachuluke bwanji Km M'TEMBO Ndy dzina lanu Lomaliza,

Ndiodala amene YEHOVA akhala M'busa wawo, chifukwa alindi malo kumwamba

uthenga uwu tumizilani kwamitundu yonse imene imamva chiyakhulo cha chichewa

k*ti iwoso aziyenda okozeka palipose

RASPBERRY FREE STORIES 15/06/2024

MABALA OSAPOLA

PART 6

Written by Mzungu wa Chilhomwe

Sponsored by:
Mrs Achumachao
Flex mng'omba

WhatsApp +27656471167 for more information

Follow us on Facebook: Raspberry stories.

WhatsApp group https://chat.whatsapp.com/GUYx6eAiuqeGLMmeSzRzRg

"Zisiye Shantel, komabe kwa nthawi yochepa chabe ndimafuna utandibweleka mapilikanilo ako k*ti umve zomwe ndikufuna kukuuza".
"Bola zisakhale zokuswa mtima wanga".
"Sindikuganiza choncho Shantel, ndipo ndili ndi chikhulupiliro k*ti uzikonda bola ukamazimva ukuyenela kuchosa maonekedwe anga, uchose zakomwe ndachokela koma tipange zamalo omwe tili". Shantel anakhala chete kenako anati.
"Kodi iwe umaoneka bwanji? Nanga umachokela kotani?". Analiponya funso Shantel kupangisa k*ti Emanuel asokomole pang'ono ndikuchosa amaliongo apakhosi kenako anati.
"Usayiwale k*ti ndiine m'mozi mwa anyamata omwe timadedwa chifukwa chometa m'mbali, ambili amatiganizila zoti ndiife achamba".
"And then?".
"Usayiwalenso k*ti kwathu ndikosauka maka tikayelekeza ndi kwanu ndi....
"Leka kulankhula mbwelela Emanuel ungauzule mkwiyo wangae pomwe unali ukundimva?". Analankhula mokalipa Shantel kupangisa k*ti Emanuel aleke kulankhula kenako Shantel anapitiliza kulankhula ndipo anati.

"Sindikufuna kuzamva mawu oziphwekesa kuchoka lelo mpaka kale, zachuma cha bambo anga zisapangise k*ti uzisise chifukwa ine mwini ndili pano kucheza nawe posatengela za umphawi wa makolo ako. Ndikamakuona Emanuel, ndimakuona ngati munthu nzanga basi ndipo zinazo zisiye. Kaya ukundimva?". Emanuel anagwedeza mutu kusonyeza kuvomela popeza panthawiyi kunja kunali kukuoneka ndipo mwambi oti nkhani ya usiku sitivomela ndi mutu unali usanayambe kugwila ntchito
"Lankhula zomwe umafuna sopano". Emanuel anakhala chete kenako anayamba kulankhula.

"Ukudziwa chani Shantel, chondisausa mtima lelo ndilankhula ndipo zomwe ndilankhule apa sizochoka pansi pa lilime k*ti nthawi iliyonse nditha kuziyiwala ayi, izi zikuchoka pansi pa mtima wanga ndipo...". Emanuel asanamal

RASPBERRY FREE STORIES WhatsApp Group Invite

21/03/2024

Momwe timabadwila tizilombo tina

Kodi mukudziwa pali tizilombo tinda tomwe kubadwa kwake timayambili m'madzi kenako ndkudzakhala pa ntunda komaso ndikumawuluka

Nthawi zambili ndimakambapo za zodabwitsa zomwe anazilenga Mulungu,

Monga momwe tawonela mumka video ka

K*t tiphuzile zambili komaso kuwona zosiyana siyana pangan share komaso like page ino

Photos from Nekhantan onekha's post 19/02/2024

Sad news😰😰

Zikuchitika Pompano ku Machinga kwa Msanama

Mkulu wina anamupempha wa njinga k*ti amugayile ndalama koma wanjingayo anayankha mwa mwano.

Apo opemphayo anamugenda mkuluyo ndi mwala mkumugwesa panjinga.

Kuloyo pofuna kupulumusa moyo wake wathawa mkuyisiya njinga yake pompo.

Apa opemphayo akuyitchola tchola njingayi.

Monga mukuwonela muchithunzimo mkuluyi ndi olumala ndipo analumala chifuwa sitima inamugunda.

Pomphanya njingayi akuyankhula mawu amvekele.

Ngati ndinapulumuka ku ngozi ya sitima sindingawope munthuso.

Komatu zafika povuta eishhh😢😢
________________________________________

Onesesani k*ti mwapanga follow page ino k*ti zambiri zisamakuphonyeni.

K*ti mupange follow
dinani apa 👉NEKHANTAN ONEKHA PA (FB)

29/12/2023

Ndikudziwa k*t ena mumadziwa komaso ena simumadziwa komaso simunavepo za somba munthu

Marmed (nsomba munthu)

Pangani like page ya nekhantan onekha k*t tizitha kucheza ndkuphuzitsana zinthu zambili za dziko lapasilino

Choyamba ndipepese k*ti k*tumiza nkhani ndinachedwerapo pa zifukwa zina komabe ndisakuchedwetseni mwadikira nthawi yaitali....

Nsomba munthu (marmeid)

Ndi cholengedwa chomwe chimakhala mbali inai munthu tikukambatu munthu wamayi pomwe pansi pakepa imakhala nsomba ndithu nkumaoneka ndimaonekedwe awiri monga nsomba mbali inayi munthu (nsombamunthu).

Chilengedwe ichi chinkapezeka kwambiri ma continet monga Europe,Asia ndi kwathu konkuno ku africa.

Ma marmeids akhala nyanja zikuluzikuli ma continent tatchulawa ndipo ali ndi zikhalidwe zawo zosoyanasiyana monga kusangalalira mvura,kusangalalira mwenzi kuwala kwadzuwa,chisangalo cha anakubala nde wina ak*ti chisangalaro cha anakubalawa kodi amagwaso nchikondi nkubeleka ana??? Eya am mr com com mW

Ma marmeids amagwaso nchikondi kawirikawiri amakhala anthu ngati inu nomwe ( the human) nkukhala ndi banja losangala mpaka kukhalaso ndi ana.

Osaiwala kupanga like page ya

Ngati mwagwa nchikondi ndi nsomba munthu ndek*ti inuyo simudzafunaso munthu wina chifukwa ntima wanu wonse umakala uli nkati mwenimweni mwa nsomba munthuyi nde ngati makonda kuwazembera akazi anu dziwani k*ti nkovuta k*ti mugwe nchikondi ndi nsombamunthu chifukwa chilengedwechi chimadziwa k*ti wachikondi wake ali pak*ti ndipo akupanga chani ndipo chilengedwechi chili nk*thekera kokusokonezani ubongo kudzera mu nyimbo....

Wina ak*ti nde banjalimatheka bwanji poti asombamunthuwa amakhala madzi??

Dziwani izi kukhala nchikondi sizitengera k*ti awirinu mudzikhala limodzi ayi komano mitima yanu idzikhala limodzi menemu ndimene zimakhalira ndi chilengedwechi...

Tsono zimakhala bwanji k*ti akhale ndi ana popeza mbali ina ya munthuyi kumakhala chinchira chasomba?????

Fetelisation..........

End of part one..
Like page..
Nekhantani onekha...

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe Area 18?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address


Area 49
Lilongwe Area 18