Team Zigege
�NABWERA KUDZAKHALA����������������
ABUSA : MUPANGE ZIBWEZI
ME : KODI ABUSA MULI NDI MA EX ANGAT INUYO?
ABUSA : AMBUYE AKUDALITSENI ATSOGOLERI
ME : OOPS!!😴😴😴
😂😂😂😂😂😂
ZINTHU 10 ZOWONA 🤣
1:Sungasuke maso ako ndi soap
2:Sungawerenge tsitsi lako
3:Sungathe kupumira mphuno pomwe watulutsa lilime lako
4:Apa wayesera kupanga No: 3
6:Pamene wapanga No :3 waona k*t mzotheka kupuma bwino bwino koma ukuoneka ngati galu🐶🐶🐶
7:Ukumwetulira panopa chifukwa wapusisidwa
8:Sunawerenge number 5
9:Wasakasaka k*ti uone ngati palidi number 5
10:Wamwetulira poona k*ti number 5 palibe 😂😂😛
03/04/2024
𝕻𝖊𝖕𝖆𝖓𝖎 𝖆𝖟𝖎𝖒𝖆𝖎 𝖔𝖘𝖎𝖉𝖜𝖆𝖓𝖚
MY WEIGHT FROM 2019 - 2024
2019: 54KG
2020: 54KG
2021: 54KG
2022: 54KG
2023: 54KG
2024: 54KG
KUMATI NDIKUKULA APA😂😂😂😂💔💔🏃😜😜😜
PLEASE MAY YOU REVIEW MY PAGE @followers🙏🙏
KOMA MMMMH ALUMU ZOMWE ACHITA INU HAHAHA ZOVUTA
😍🥰🥰❤️😜😜🇲🇼🌹🌹🌹🌹🌹🌹
KODI CHIBWEZI CHOYAMBIRIRA CHINALI CHA NDANI😉😉😂😂😂@followers@followers
KOMA ANTHU MUMAKHALA SILIYASI EEEEEEEH HEART BREAKYOMWEY MPAKA KUTSEKULA MIMBA HMMM NANGA INAKAKHALA HEAD BREAK MUNAKATANI🙄🙄😜😜😜💔💔💔😂😂😂😂
EYA TIVANEPO APA ALAMU ANU AJA NDI..........
❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
🌹🌹🌹🌹🌹🌹🌹🌹
💐💐💐💐💐🌷🌷🌷🥀🌼
Shakin @followersShakin RoshanShakin Roshan
NIDKUNGOFUNAKO MA COMMENT 100 OKHA BASI @followers LET'S GO!!!!
TAMUTCHURENI ZANU AMENE AMAKONDA ZIGEGE NGATI INE TIMUONE
🤣😂😂😜😜
TITUMIZE YA ZIGEGE KODI???
🤣🤣🤣💔💔💔@followers@followers
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Kawale 2 Near Kamuzu Institute
Lilongwe Area 18
