Friends Of Zamkutu Bypass LL
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Friends Of Zamkutu Bypass LL, Health/Beauty, Lilongwe.
WAKA WAKA MARKET NOMORE Friends Of Zamkutu Bypass LL Mikozi
Mwana wamzako akachita zabwino kumamuyamikira 💪
Miyambi komaso malangizo a ulere kkkkkkFriends Of Zamkutu Bypass LL
18/04/2026
Ndikudusa mu Rumphi, mwiniwake palibepo, bwanji ndimuchangamutse nditenge iyaaðŸ¤
Dear MALAWI POLICE SERVICE (MPS) Kodi kuzepula mkazi wa zaka 15 koma wa mwana kale ndi Mlandu?
25/03/2026
Oweluza milandu m’boma la Ntcheu, His Worship Pleasant Sichali, alamula Mphatso Phiri wazaka 19 kuti akakhale kundende zaka zitatu kaamba kolowa m’nyumba ndikuba nyemba za makilogalamu 25 ndi jombo zonse za ndalama zokwana K127,000.
Pa 14 March 2026, mwini nyumba Miriam Mwase anachoka kokonzetsa chitseko cha nyumba yake chitaonongeka, koma pobwerera anapeza nyemba ndi jombo zitasowa m’nyumba.
Atakadandaula kwa agulupu a Kadzakalowa, ananena kuti anaona Mphatso pafupi ndi nyumbayo ndipo atafunsidwa, anavomera kuba katunduyo yemwe anapezeka kunyumba kwake ndikukamutula kupolisi.
Kotero bwalo la milandu lero lapeza Mphatso wolakwa ndi kumulamula kukhala kundende zaka zitatu, pomwe nyemba ndi Jombo zabwezedwa kwa a Miriam Mwase.
Wolemba Bertha Banda
Ku Dedza wakuba waphedwa ndi anthu ammudzi tiyeni kwathu kuno Ku Bypass tiziwalondoloza a rent,ana,ndi amzathu omwe timakhala nawo moyandikana nawo Kuti moyo wawo WA tsiku ndi tsiku zimakhala bwanji chifukwa Ena omwe akumabawa ndi omwewa ana athu,A rent athu, Amzathu ocheza nawo! Tiyeni ngati tikuwakaikira tikawaneneze Ku Police yomwe tilinayo pafupi ndipo akakusungirani Chinsinsi!
22/03/2026
From 6miles Round About To Gate Way Mall Mchinji Round About
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe
