Macheza pachizumulu
Macheza
mwazuka bwanji?
Kodi kuchizumulu ko zikuti bwanji kod zampira player zitheka bwanji kusayinila mtimu awili pakamozi yekha ku super yekhaso ku yofu kulikoma kodi afamu akumeneko malamulo amawaziwa apena zalowandale???
Azisogoleli athu kuganiza kumawavuta makamaka uyu ndani uyu eshiiiii
Ndipepese kwanose amene ndinakunamizani kuti ndizakutengani banja kungoti ndinakuyankhulani mwachangu banja ndi inu nomwe
Ukamati ndapeza weniweni sopano okukonda masewela wasiya osaziwa kuti mzako yemwe ukunenayo pamene wasiyila iwe masewela ndi pamene mzakoyo amayambila masewelawo. osamapusa
Mafuso omandi fusa kuti ndizakhala nacholiti chibwezi zichepe pomwe inu kuku funani mkumakana chomwe mkufuna ndchani kod?🙋
Kufela fungo laziko lapasi mtundu wamalawi lelo siyiziii....
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Lilongwe
