Tiwonge Chirwa

Tiwonge Chirwa

Share

We will be discussing issues to do with relationships and people living with HIV.

That we should not look down on ourselves, but hold on to our vision so that we should achieve our goals.

06/09/2022

Hello my beautiful people, lero ndafuna kuti ndiyankhe mafunso omwe ena mwa inu muli nawo ofuna mayankho kuchokera kwa ine

M***a kundifusa ma funso okhudzana ndi umoyo wanga, kumbali ya my HIV status komaso kumbali ya wokondedwa wanga

Photos from Tiwonge Chirwa's post 31/08/2022

On 20th August what a memorable day.

Hello guys ndangofuna kuthokoza Mulungu pa zomwe wandichitira, pali zinthu zina mwa ife tokha sizitheka koma Mulungu akalowerelapo zimatheka, just want to encourage someone today kuti being HIV positive sizitanthauza kutha Kwa moyo wako ayi, koma chiyambi cha moyo wina, ineo zoti ndidzakula ndikupeza mamuna wa negative honestly sindinkadziwa koma alipo amuna oti amakukonda ndi momwe ulili. Much love my husband.

Tiyeni tisamadzikaikire pa chilichonse coz ndima ARV nditha ndipo ndinakwanitsa kukwatiwa moti panopa ndine Mrs SebastianπŸ₯°πŸ₯°πŸ₯°

Koma zinali zosangalatsa kwambiri moti chilichonse chinayenda bwino

Photos from Tiwonge Chirwa's post 24/08/2022

Having lunch at Sunbird hotel

Am honored to attend a Southern African Regional Students & Youth Consortium on Sexual Reproductive Health

15/08/2022

5 days to goπŸ™πŸ™

14/08/2022

Hello my pple, pa dzana paja timati Chaka cha mawa, mwezi wa mawa, week ya mawa pano tikuti tatsala ndi masiku ochepa chabe( 6days).

I really thank God for this special day patokha sitingathe zikasowekera Mulungu mwini wake kuti zikatheke komaso zikayende bwino.

Thanks to my husband to be for the love u gave me and for everything you have been doing and u r still doing them sindikuchitenga ngat chizolowezi koma kwa ineyo ndi chisomo chokwanila ndimakukonda Tobias Sebastian ❀️❀️.

Can't wait to see you guys ku wedding yathu ndipo tikakhala okondwa tikakakuonani

Photos from Tiwonge Chirwa's post 09/08/2022

On 30 july tinali ndi bridal shower koma zinali bwino moti tikungothokoza Mulungu kuti anali mbali yathu.

Pa 20 August pano tikamalize zimenezi much luv my pple

06/08/2022

U are all invited to our wedding, it will be a joyful and entertaining day coz ndikakhala ndikulimbila pamaso pa anthu onse saying "I Do" and my name will change to "Mrs" πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

But I really thank God for everything coz he is always there for us and he has never disappoint us no matter how had the situation maybe but he is a faithful God and God of possibilities.

28/07/2022

A day after tomorrow πŸ’ƒπŸ’ƒπŸ’ƒπŸ’ƒ

28/07/2022

It has been God since day 1, we started ngati zachibwana till last year pa 18 December when he proposed to me.

It was like a dream I couldn't believe what my eyes were seeing and what my ears were hearing, I was so happy and I then realized that some pple love the way I are no matter am HIV positive but still he did not look back and he encouraged me in so many ways

22/07/2022

CAN πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

22/07/2022

# I CanπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Area 46, Chinsapo 1, Kachere
Lilongwe
0000