Healthy Herbs Clinic
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Healthy Herbs Clinic, Health/Beauty, T/A Njolomole, Ntcheu, Lilongwe.
28/12/2025
*ENDOMETRIOSIS*
✍🏽Endometriosis ndi nthenda la zomatilira/zotupa zomwe timapezeka kunja ndi nkati mwa chibelekero, njira yodutsira mazira, kopezeka mazira komanso malo ena mthupi la munthu wa mkazi
Ili ndi vuto lomwe akazi ambiri akuvutika nalo. Nthawi zambiri amayesa kuti mwina ndi fibroids kapena ovarian cyst koma ayi akapanga scan samazipeza.
Ngati achipatala anakuuzani kuti mulibe fibroids komanso ovarian cysts koma mukuvutikabe ndi:
* Ululu nchiuno,
* Period yayitali pena yayifupi,
* Kupweteka pogonana,
* Kusabeleka,
* Kupweteka kodetsa nkhawa mwezi uliwonse.
* Kupweteka pokodza.
* Kutaya magazi ochuluka nthawi ya period.
Dziwani kuti ndi Endometriosis.
✓Zoyambitsa vutoli ndi zambiri, zina mwa izo ndi izi:
1. Kusapanga balance kwa ma hormones.
2. Kubwelera kwa magazi kupita ku njira zina mmalo motuluka kunja nthawi ya period.
3. Opaleshoni
*NOTE:*
Amayi ambiri akulephera kubeleka chifukwa cha vutoli. Mankhwala tilinawo mitundu iwiri
Mankhwala alipo othana ndi vutoli.
*Healthy Herbs Care ☘️*
19/11/2025
*TO BREAK A LOVE RELATIONSHIP*
You will need two candles: each one will represent a member of the relationship.
With a pin, write the full names on each of the candles respectively.
On a brown piece of paper write the above magic words.
Be sure to burn the paper with the flame of the two candles and store the ashes in a piece of aluminum foil.
Place the aluminum foil inside an old shoe and add some of your own urine.
Take the shoe to a busy place, such as a park or shopping mall.
Drop the shoe, turn around and leave the place without looking back.
19/11/2025
https://chat.whatsapp.com/GXh66T3W7tY9dXPNbacThc?mode=hqrt3
HEALTHY HERBS CLINIC 2 ☘️ WhatsApp Group Invite
24/10/2025
IMMUSANTE
Herb iyi imathandiza mavuto osiyanasiyana monga:
- Chitetezo Chochepa nthupi
- HIV/AIDS
- TB
- Cancer ya mtundu ulionse
- Mukudwala kapen thupi likungotha herb yanu iyi
- Mukufuna kuziteteza ku matenda mwerantuni herb iyi
- Mwafooka , herb yanu iyi
- M'nthenda za mgonagona gulani herb iyi.
- Amathetsa matenda omwe akufuna kuyamba.
- Mukudzikaikira kuti amwina mwatenga Matenda mutatha kugonana( HIV/AIDS, STIs, UTIs) imwani herb imeneyi pasadathe 24 hrs
K 60,000 ONLY
Healthy Herbs Clinic ☘️
23/10/2025
https://chat.whatsapp.com/GXh66T3W7tY9dXPNbacThc?mode=ems_copy_t
HEALTHY HERBS CLINIC 2 ☘️ WhatsApp Group Invite
08/10/2025
ULCERS
-Ma asazi ndi mabala, mabala awa nthawi zambiri amavuta kuchira ndipo amasautsa kwambiri.....akakhalikira amayamba khansa ndipo ena amatha kumwalira.
NJIRA ZACHILENGEDWE
-Pezani papaya osapsya koma akhale okhwima.
-Duladulani ma pieace ang'ono ang'ono musasende komaso osachotsa nthangala.
-Tengani ma piece anu iyikani mu container mutsuka bwino mukatelo thilani madzi alekeze momwe mwalekela mapapaya aja
-Vindikilani kwa masiku awiri after this ndiye muvundukule,
-Mukavundukula Chotsani mapiece aja ndi nthangala zomwe, mutsale madzi aja basi
DOSANGE
-Mudzimwa madziwo
Cup imodzi mawa masana ndi madzulo,
Mukatelo mudzachilitsidwa kwa thunthu kumbali ya ma ulcers.
Ma herb a ma asazi aliponso inbox
Healthy Herbs Clinic ☘️
01/10/2025
PELVIC INFLAMMATORY DISEASE(PID)
Iyitu ndi Nthenda yomwe imakhuza Ubeleke wa Zimayi yomwe imayamba kamba k**a Bacteria.
ENA MWAMA BACTERIA OMWE AMAYAMBISA PID
1. Chlamydia trachomatis
2. Neisseria gonorrhoeae
3. Mycoplasma genitalium
4. Anaerobic bacteria (Bacteroides & Peptostreptococcus)
Ziwani kuti ma Bacteria omwe ndatchulawa ndi aja amayambisaso Nthenda monga Chizonono ndi Mauka mwachidule nditha kunena kuti Nzimayi amene ali ndi PID atha kukhala zoti anatengapo Chizonono kapena ali nacho kumene.
ZIZINDIKIRO ZOMWE TINGAZIONE NGATI TILI NDI NTHENDA YA PID
1. Kuwawa kwa Chiuno ndi Nsana
2. Chikadzi chafungo
3. Kumva kuwawa pokodza
4. Kumva kuwawa pokazinga Chips
5. Period yosapanganika/yosalongosoka
6. Kumphwanya kwa Nthupi
7. Nseru ndi kusanza
8. Period yambiri/Yokhuthula
9. Penga kumazimva ngati mwaima
ZOMWE ZINGAKUGWELENI MUTANGOISEKELERA PID
1. Kuvutika kutenga Mimba
2. Nthenda ya Nsana ndi Chiuno
3. Mimba ya kunja kwa Chibelekero (ectopic)
M'MENE TINGAPEWERE NTHENDA YA PID
1. Kusiya kukazinga Chips
2. Kukazinga chips mutavala mask
KODI NTHENDA YA NTOPOLAYI TINGATHANE NAYO BWANJI???
Tikapita ku Chipatala timakhala tikumandila ma Antibiotics monga:
1. Doxycycline
2. Ceftriaxone
3. Azithromycin
4. Metronidazole
Pomwe ena amachira akalandira ma Antibiotics amenewo pali ena samachira ena zimangozizira ndikuyambilanso, Omwe mwakhala mukulandira treatment ya Chipatala koma kusintha kwenikweni palibe ziwani kuti ma Herbs ali ndikuthekera kothana ndi nthenda zotero mpaka kutha. Gulani *Lukol tablets* lero
Healthy Herbs Clinic ☘️
01/10/2025
NAMWARI MKHWINYATA
Awa ndi masamba omwe ukuwagunda amafoota or kunyala ngati akuuma kenako amabwereranso
Tikupanga ma post ake cholinga kuti mugwiritse ntchito asanasowe chifukwa amasowa nthawi ya dzuwa yomwe ikubwerayi
-Pangani check post ena mbuyomo mupeza kagwiritsidwe kake ntchito zina
Pa post ino tilemba zinthu zina
-Kwa omwe mukufuna kuchotsa tsoka, minyama, mwai, wachikondi, kukonderedwa ngakhale business ndi ntchito imene.Tengani masambawa kuika madzi mkumasamba
-Tengani masamba mkuika mmafuta obzola mkudzula
-Tengani masamba mkuika muzakudya za Mamuna wanu
>Musankha njira yomwe mukufuna ndi zomwe mukufuna
-Azimai muk**apanga choonde aoneni kaye mukuwapangirawo....... Ena mupezeka m'malo mokukondani angothetsapo chabe, ena m'malo mokukondani angopeperapo chabe
Azibambo njira iyi nanunso m***a kupanga
Azibambo omwe mwadyetsa konda ine mubwere Ku inbox mkupatseni remedy yosulutsa konda ine chifukwa azimai nde ma remedy a konda ine ndie ndawapatsa kwambiri🤣
Mongokumbutsana, pagroup pano timathandizana ndi kutsatirana bwino polemba uthenga ku WhatsApp osati kuimba foni or inbox ya Facebook choonde ayi 0997374475
Healthy Herbs Clinic ☘️
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
T/A Njolomole, Ntcheu
Lilongwe
