Small wifey

Small wifey

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Small wifey, Health/Beauty, Lilongwe.

23/07/2025

Happy birthday handsome Eli πŸ’™
Uyuso titha kukhana eti ?πŸ™„

22/07/2025

Ndifuseko ine ndi waxy kay tingakhalane eti πŸ™„ kapena ayi

20/07/2025

Ine ndikuti Miracle Vic Chinga ndi pangolin 😊

15/07/2025

South Africa Loading ✈️

11/07/2025

Congratulation Banbo a Mia mr Ndidzasangalala hit Maker Rash Ley

Photos from Small wifey's post 09/07/2025

Morning
Mwaonela kale welcome to maula prison ngati . Tiyeni ku YouTube konko πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ”₯

07/07/2025

Wina kukanena ku police kuti Ching'aning'ani wandiluma pa ndewu Mano ake atiwo ?πŸ™„Nsambi basi . Hy Daddy ching'axy ❀️

07/07/2025

Your beautiful model Small wifey
Tsiku lanu linali bwanji?

07/07/2025

Madzulo uno nsima ndikadya kwa miracle chinga ☺️❀️

07/07/2025

Kodi there is pipo omwe they still said this is fake page . Oh ok it's fine kwa ineyo mzosadandaulisa kwambili.
πŸ”‡πŸ‘‡
Ineyo mnaziwa mochedwa kuti athu akunnndiziwa nde mmene ndimkati ndisegule page mnapeza athu ena asegula ma page ochuluka kwambili that's why muzaone Mikozi komaso Makosana sapanga Tag akaposta za ine coz palibe page ya. Original ya Small wifey . So as l said mukaberedwa ndalama it's not my fault ndipo zisazandikhuze . Page tasegula kumene and you can ask pipo yomwe. Takumana dzulo mu sungwi mu .
Follow me on
1. Twitter
2. Facebook
3. Instagram
4. Tik Tok
5. YouTube

Love you all
Masana anu ali bwanji?β˜ΊοΈπŸ˜ΊπŸ…

07/07/2025

School Days πŸ’—
Morning 🌞

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Lilongwe