M'titi.Mw
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from M'titi.Mw, Health/Beauty, Liwonde.
27/05/2024
Nyimbo yabwinodi imaziphusha yokha
Ndikudabwa kuti Mikozi ndi Makosana sakuwapopa bwanj adha awa pa achievement yawoyi.
Komano penanso ndikudabwa kuti ma fans ake ndi akutiko amene amaonela kuti ifike ma views choncho chifukwa nyimbo yokuti ili 981k kusala ndi 19k kuti ifike mita anthu sakuiziwa bwanj.
Kayo withu watizizimusa
https://youtu.be/QrdOl3dc2J4?si=DREMaez_1Ff_jESO
03/04/2024
Munthu Nd chimwene wake kuthilana battery munyumba ya makolo awo ana akukasungu sazava vungan # tikugayilen🤸😂
07/03/2024
Mwayi wanu boys bwelani mupeze otchindana naye lero kwinaku akukupasani ndalama 0882643660
25/01/2024
Eeshh💔
Ingosindikizan mau awa 👉Hilco's kenako pangan like 👍 page, ndipo mulandila nkhan yonse yomwe yamuchitikila mtsikan wa zaka 22 ameneyu🙌
17/01/2024
Zikuchitika pompano
M'titi. Mw
For more😂😂😂😂
04/01/2024
04/01/2024
KODI MUKUDZIWA?
Choyamba ma star landirani ma ulemu kulikonse komwe muli mu chaka cha tsopanochi nanga mwachilowa bwanji? Monga team admin member Pavarotti mphamvu Zokhazokha ndipo tipitiriza kuchita mmene timachitira osafooka👇👇
1. Nkhono imapumira kumapazi ake.
2. Mphuno ya munthu imatha kukumbukira fungo la zinthu zosiyanasiyana zokwana 50,000.
3. Udzudzu Uli ndi mano 47
4. Pafupifupi theka la mafupa athupi lanu lili kumapazi anu
5. Mafunde a muubongo atha kugwiritsidwa ntchito poyendetsa sitima yamagetsi
6. Abuluzi amalumikizana kudzera njira ya push-ups
7. Kununkhiza fungo lama apulo/apples kapena nthochi kungakuthandizeni kuchepetsa thupi.
8. Anthu samayetsemula m'tulo chifukwa ubongo wawo umatsekereza njira yotchedwa reflex yomwe imachitika mwa automatic munthu akafuna kuyetsemula
9. Mphuno ya munthu imatha kukumbukira fungo la zinthu zosiyanasiyana zokwana 50,000
10. Amphaka amatha kupanga mau okwana 100 polira mwakasinthasintha
11. Nyama zomwe zimaikira mazira sizikhala ndi nchombo
12. Munthu osuta sachedwa kumera imvi kusiyana ndi amene sasuta( kupatula zaku mtundu)
13. Ku South Korea kuli number ya emergency yomwe munthu amaimba akaona kuti pali winawake yemwe akupanga zaukazitape ndipo number yake ndi 113
14. Manyi ansomba ya whale 🐳 amagwiritsidwa ntchito muma perfume ena
15. Carrot siwabwino kwa akalulu
16. Munthu akagona tulo samva fungo la chilichonse or chitakhala choola
17. Nzosatheka kuwerenga tsitsi lanu
18. Nzosatheka kupumira m'mphuno mutatulutsa lilime.. ngati zingatheke mungokhoza kumapuma ngati galu kapena bakha komanso mopanikizika.
19. Mkwiyo umafooketsa chiwindi ndipo sichigwira bwino ntchito moyenera mukakwiya
20. Kudandaula kumafooketsa m'mimba komanso mumakhala pachiwopsezo chodwala ma ansazi (ancers) kapena kuti zilonda za m'mimba
21. Mantha amafoola mtima ndipo sugwira bwino ntchito.. Umagunda kwambiri kusiyana ndimmene umagundira poyamba
22. Chisoni chimafoola mapapo. Mukakhala pa chisoni mapapo anu sagwi
24/11/2023
A Frenchman traveled all the way to Ivory Coast in search of a nanny who used to take care of him 38 years ago .
He couldn't hide his happiness after meeting the elderly woman. He gave her 10 million francs and allocated a monthly salary to her.
His retired father once worked in Ivory Coast before leaving his job and relocated to France
12/03/2023
*ZINA UKAWONA*
Mtsikanayu ndi Agent wa Airtel money komaso Mpamba koma pa malo ake pakumadzadza azimuna popeza adapeza njira yabwino yoyitanila ma customers
Style ndi wekha pa Town, bola iwe zako zikuyenda basi
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Liwonde
