Annie Tuweni Chauya
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Annie Tuweni Chauya, Health/Beauty, Zomba, Thondwe.
26/08/2023
Idont have any stress .
Feeling gud kumuzi kuno .God is in control
Musazaope omwe ali kutsogolo kwanu ayi inu muzaope omwe ali mbuyo mwanu
Abale ndi alongo omwe madela anthu kukugwa mvula tiyeni tisamale ngati mukukayikira nyumba yanu chonde .
Chonde musagonepo or musakhalemo kapempheni malo komwe kukuoneka kuti kulibwino or ku school kagoneni or ku police.
Pomaliza pepani nonse mwakhudziwa ndi ngozi imeneyi ya madzi (Freddy cyclone)
Anthu ambili amafuna kupephera nthawi imene ali ndimavuto .monga kusowa ntchito ,banja,ngakhale umphawi .
Koma Mulungu amatisunga ndicholinga kuti tilape ndikupanga chifunilo chake ndipo amatipatsa moyo daily posayang'ana machimo anthu
17/11/2021
Local village girl ilike the way iam ?and i praise his almighty Lord for free life
Dziko lapansi chili chonse chikunthera pa social media
(Facebook )
Defference between life and Moyo
Life is so simple while
Moyo siopweka k*k
Just want to thank all those who likes my page once again thank you idont take it as grated
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Website
Address
Zomba
Thondwe
