Faxy
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Faxy, Health/Beauty, falidhassan6@gmail. com, Pietermaritzburg.
11/09/2024
Following
10/09/2024
Mphunzitsi wina analowa m’kalasi mwake ndipo anapeza mpando umene anayenera kukhala utapachikidwa padenga. Anayang'ana ana asukulu ndikumwetulira. Popanda kunena chilichonse, adapita pa bolodi ndikulemba kuti:
(Mayeso - 15 min, 30 marks.)😂😂
(.Funso loyamba Q1.) Werengani mtunda wa pakati pa mpando ndi pansi mu masentimita (1 Mark).
(Funso lachiwiri Q2.) Werezerani momwe mpando ukukhalira padenga, onetsani momwe mumagwirira ntchito (1 Marko)
(funso lachitatu Q3 )Lembani dzina la wophunzira amene anapachika mpando padenga ndi anzake amene anamuthandiza. (28 Marks).
Chitani like kapena follow kuti zisakuphonyeni zambili
20/07/2024
M'malawi sazatheka basi
12/01/2024
nayeso ndimunthu amafunika kunjoya
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Falidhassan6@gmail. Com
Pietermaritzburg

11/09/2024